Hymn 525 Afike masiku treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 525 Afike masiku Afike masiku akuti anthu onse Adzamva mawu anu ndi kutsata inu nokha; Muwale mtima mwawomo, Adziwe muwakondanso; Kopani anthu abwere kwa Inu, Kopani anthu abwere kwa Inu.