Hymn 1085 “Khala mwa Ine,” ndinu mwini mphamvu, December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1085 “Khala mwa Ine,” ndinu mwini mphamvu, “Khala mwa Ine,” ndinu mwini mphamvu, Mundithandize ine ndikafoka; Mzimu Woyera andiululire Zoona zanu m’mtima mwangamu.