Hymn 1085 “Khala mwa Ine,” ndinu mwini mphamvu, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1085 “Khala mwa Ine,” ndinu mwini mphamvu, “Khala mwa Ine,” ndinu mwini mphamvu, Mundithandize ine ndikafoka; Mzimu Woyera andiululire Zoona zanu m’mtima mwangamu.