Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 453 A! MULUNGU

  1. Home   »  
  2. Hymn 453 A! MULUNGU

Hymn 453 A! MULUNGU

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 453 A! MULUNGU

 

A! MULUNGU
A! Mulungu
Anatuma mwana wake
Uja, ndiye Yesu

Anabadwa,
Anabadwa
Ndi Maria Mbeta ija
M’Betlehem muja.

Ndi angelo,
Ndi angelo
Anaimba: “Ndiye Yesu
Mpulumutsi wanu.”

Alanditsa,
Alanditsa
Ife anthu muzoipa
Zonse tazichita.

Yesu Mfumu
Yesu Mfumu,
Timagonja, mutisunge
Moyo wathu wonse.

Mutisuke,
Mutisuke
M’mwazi wanu, tikakhale
Ana anu tonse.

Post navigation

Previous: Hymn 452 MLUNGU, Inutu,
Next: Hymn 454 TAONANI, m’kholamo,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 417 M’manja a Yesu wanga
  • Hymn 1132 Mlungu adzandilandila,
  • Hymn 23 Mvera mtima wanga ‘we
  • Hymn 464 Yesu atiuza tiyambemo,
  • Hymn 1384 Mphamvu yake inalenga
  • Hymn 397 Yesu Mbusa, mutimvere,
  • Hymn 456 ANA inu, ana inu,
  • Hymn 863 A! maliro m’Mpingo mwanu kulirira ‘balewo
  • Hymn 74 Ndipereka zanga zonse
  • Hymn 1289 Ndinasokeratu kutaliko,
  • Hymn 49 Ndi ife akudziwa
  • Hymn 497 TILIKUIMBA nyimbo yomweyi,
  • Hymn 1101 Ngati mtima sumakonda
  • Hymn 559 Usikuwo woyerawo!
  • Hymn 256 NGATI mtima sumakonda
  • Hymn 967 Mbuye, ndapangana
  • Hymn 292 NDIPULUMUTSENI Mbuye,
  • Hymn 381 Chakudya changa chabwino
  • Hymn 335 Mtembenuke mtima wanu,
  • Hymn 291 Ndi milomo yathu iyinso njanu,
  • Hymn 908 Ndikonda kuganizirabe
  • Hymn 1582 Konda dzinalo la Yesu
  • Hymn 1333 Idzatu kwa Yesuyo,
  • Hymn 917 Ndi nkhondo ikaleka
  • Hymn 99 Tsopano ndimwona Iye
  • Hymn 385 SINDILI woyenera ’ne,
  • Hymn 278 TITHAŴIRENJI ifetu
  • Hymn 93 Mverani mbiri yozizwitsa
  • Hymn 175 A! MBUSA wathu amvatu
  • Hymn 275 NTHAWI yathu yafikatu,
  • Hymn 348 CHIKHULUPIRIRO chathu
  • Hymn 215 Choka, choka,
  • Hymn 1805 Anafa m’mvula muja
  • Hymn 415 Tidzalandirabe komwe
  • Hymn 1611 Nadzuka m’mandamo
  • Hymn 1662 Msandipitire, Yesu,
  • Hymn 79 Mlendo ali pakhomo,
  • Hymn 840 Ambuye munapatsa tsiku
  • Hymn 1533 Ndipatsa inu mtimawu,
  • Hymn 472 YESU, ndikabwera
  • Hymn 981 Tiyeni Akristu,
  • Hymn 315 Munagwa pa Atumwiwo;
  • Hymn 1409 Kodi mufunatu Yesu?
  • Hymn 1775 Oonadi mtima,
  • Hymn 343 Auke,
  • Hymn 1717 Mtima wangawe, uyenera
  • Hymn 1443 Ambuye Yesu anatsira
  • Hymn 493 DZUŴA li
  • Hymn 1282 Ndilinkudza kwa Ambuye,
  • Hymn 9 TAMANI Ambuye,
  • Hymn 73 Mu ulemerero tidzakhala m’yaya,
  • Hymn 3 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 939 Ambuye andisunga
  • Hymn 921 Komwe Mbusa kwawoko
  • Hymn 1129 Mbuyanga Yesu, ndikapanda Inu
  • Hymn 1353 Ambuye Yesu, Inutu
  • Hymn 51 Mbuye dalitsani Afrika,
  • Hymn 443 M’MAŴA tizifesa
  • Hymn 497 Yesu andikonda ine,
  • Hymn 795 Sitinanyalanyalaza

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version