Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 939 Ambuye andisunga

  1. Home   »  
  2. Hymn 939 Ambuye andisunga

Hymn 939 Ambuye andisunga

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns

Chichewa Believers Christian Hymns

Hymn 939 Ambuye andisunga

 

Ambuye andisunga

M’chifundo chachikulu;

Zisoni zisanduka

Chimwemwe cha Mulungu.

Dzanjalo ndilitama

Ndi mtima wachifundo,

Mpakatu kwawalitsa

Ku Dziko la Mulungu.

Post navigation

Previous: Hymn 938 A! Yesu Bwenzi langa
Next: Hymn 940 Ndamvatu kuti tifika komweko

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1416 Mbuye wanga ndilikumva,
  • Hymn 1423 Oipa inu nonsetu,
  • Hymn 554 Iye ndani pamtanda
  • Hymn 1832 Za m’mdima, imfa, nkhondo ndi zoipa sindiopa;
  • Hymn 203 Pamtandapo, pamtanda,
  • Hymn 116 MBUYE, Mawu anu
  • Hymn 1141 Pakulekana ifetu
  • Hymn 1758 Poti Mulungu wathu
  • Hymn 1520 Mbuye, Mawu anu
  • Hymn 880 Bwenzi lathu ndiye Yesu
  • Hymn 887 Pakupempherera
  • Hymn 133 NSEMBE yake ya Kaini,
  • Hymn 1510 Mtume tsopanoli
  • Hymn 1239 Ndipo pakuima phe!
  • Hymn 1476 Mipingo iyo idzatu,
  • Hymn 1748 Ambuye tsopano lino,
  • Hymn 994 Limba mtima mbale wanga,
  • Hymn 1857 Ndinagona mwa zoipa,
  • Hymn 585 Alanditsa,
  • Hymn 268 POKHALA mtendere mu mtimangamu,
  • Hymn 236 NDIDZIWITSITSA
  • Hymn 1456 Pakuti anthu akumvera
  • Hymn 397 Yesu Mbusa, mutimvere,
  • Hymn 278 TITHAŴIRENJI ifetu
  • Hymn 1582 Konda dzinalo la Yesu
  • Hymn 1778 Angelo kwezani
  • Hymn 1688 Mulibe m’mandamu,
  • Hymn 576 Kondwerani nonsenu
  • Hymn 1003 Kanganani nkhondo yanu
  • Hymn 48 IMFA ya Mwana wa Mulungu,
  • Hymn 110 MZIMU ndi mtogoleri
  • Hymn 174 YESU wathu Mbuyeyo
  • Hymn 1392 Mlungu kuona athiratu
  • Hymn 936 Ukatha moyo wanga
  • Hymn 247 Tsono poukanso
  • Hymn 21 Mbuye mtsitsimutse!
  • Hymn 338 ’TATE wa Kumwambako,
  • Hymn 1385 Anatsogolera kale
  • Hymn 1183 Adalitsika, indetu,
  • Hymn 235 Kumwamba ndikaimbanso
  • Hymn 519 Mverani, aimba anawo,
  • Hymn 863 A! maliro m’Mpingo mwanu kulirira ‘balewo
  • Hymn 1575 Tifuna kuti komweko
  • Hymn 193 A! Kumwamba
  • Hymn 951 Ndi kale lonse mnandisunga ‘ne;
  • Hymn 423 MUNENE Mbuye, ’nenetu,
  • Hymn 1846 Mtima wanga uyamike
  • Hymn 696 Ufumu wake udalitsa
  • Hymn 1151 Pomulambira Yesu Mbuyanga,
  • Hymn 648 Mulungu wa Kumwamba,
  • Hymn 1411 Yesu akuitanani
  • Hymn 664 Komwe asauka anthu
  • Hymn 1622 Anthu onse amlambire
  • Hymn 158 Mzimu, mlonge m’mtimamo
  • Hymn 1052 Ndilira mtima wotamanda
  • Hymn 1676 Kondwerani dzuwa lino Aleluya,
  • Hymn 745 Anatifera nsembe Iyeyo,
  • Hymn 322 PAKUYITANIDWA munthu pa dziko ino,
  • Hymn 924 Kodi uli ndi chisoni
  • Hymn 1227 Ndiyamika Mbuye wanga

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version