Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 447 OYAMIKA Mlungu m’bwere,

  1. Home   »  
  2. Hymn 447 OYAMIKA Mlungu m’bwere,

Hymn 447 OYAMIKA Mlungu m’bwere,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 447 OYAMIKA Mlungu m’bwere,

 

OYAMIKA Mlungu m’bwere,
Zamasika mudzayimbe;
Dzinthu dzathu takolola,
Sidzionongeka m’minda.
Mlungu Mlengi asamala,
Zotisowa akonzera;
M’lowe m’nyumba ya Chauta.
M’kweze nyimbo zamasika.

Dziko lonse n’la Mulungu,
Kuti lim’balire dzinthu;
M’munda zonse zimamera,
Zakukoma ndi zoipa.
Mmera udza, bwino ngala,
Maso omwe amakhwima;
Mutilole, mwini dzinthu,
Tikakhale dzinthu dzanu.

Adzabwera Mbuye wathu,
Kukolola dzinthu dzake;
M’munda mwake akachotse,
Minga ndi zoipa zonse.
Adzatumanso angelo,
Minga akaponye m’moto;
Koma tirigu amsunge,
M’nkhokwe yake nthawi zonse.

Post navigation

Previous: Hymn 446 YAMIKANI nonse ’nu,
Next: Hymn 448 CHIFUKWA cha zokoma mtima zonse zaulelezo,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1117 Ndifuna Yesuyo
  • Hymn 92 KONDA dzinalo la Yesu,
  • Hymn 1190 Aleluya, mlemekeze,
  • Hymn 311 Tifuna kuchita chifuniro chanu,
  • Hymn 956 Mbuye munditsogolere,
  • Hymn 792 Dzuwa la Mulungu
  • Hymn 544 Zoopsya sitidziwapo
  • Hymn 103 Bwenzi lathu ndinutu,
  • Hymn 66 Chisomocho chachotsadi
  • Hymn 157 Mbuye, Mzimu Woyera
  • Hymn 1605 Yesu, dzina lokondwetsa
  • Hymn 248 Pena pakufadi,
  • Hymn 1056 Mkhalidwe wanu mundipatse,
  • Hymn 721 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 267 AMBUYE, thandizenitu
  • Hymn 530 Munaneneratu mawu a moyonso
  • Hymn 932 Munabvala thupi lathu,
  • Hymn 202 Timpemphere kutipatsa
  • Hymn 1379 Mulungu yemweyo
  • Hymn 1249 Tsirizani ntchito yanu
  • Hymn 650 Tikondwa tonse ndi kukuthokazani Nu
  • Hymn 1680 Aleluya, Aleluya, Aleluya!
  • Hymn 19 Mbuye mtsitsimutse
  • Hymn 36 Nyengo ifika, chenjera!
  • Hymn 629 Tinayenda muli mdima
  • Hymn 145 Kale ndinafuna
  • Hymn 953 Ichi chindisangalatsa
  • Hymn 623 Mbuye, tikuthokozani,
  • Hymn 237 Munasiyatu
  • Hymn 1448 Yesu ndiye Bwenzi lanu,
  • Hymn 411 Yesu adza kukundika
  • Hymn 1109 Pamene ndisauka,
  • Hymn 133 Yesu watidzera, watidzera,
  • Hymn 961 Mbuye anatiitana
  • Hymn 387 Tikutha kupemphera,
  • Hymn 1765 Zoonazi amithenga
  • Hymn 383 KASUPE ali wodzaza
  • Hymn 752 Chakudya chakumwambachi
  • Hymn 1562 Mzimu Woyera, mudze mumitima mwathumo,
  • Hymn 958 Ndikalowa m’mtsinje muja,
  • Hymn 1520 Mbuye, Mawu anu
  • Hymn 1459 Ambuye mulowetse
  • Hymn 1736 “Senzani mtanda wanuwu.”
  • Hymn 420 FESANI mbewuzo,
  • Hymn 1315 Ambuye ‘naitana ‘ne:
  • Hymn 399 M’KHOLA mwa ng’ombe ku Betlehemu
  • Hymn 471 YESU Mbuye ’Nu wofatsa
  • Hymn 219 YESU Mbuyetu, mwafera
  • Hymn 481 Yesu wa Kumwamba,
  • Hymn 413 ZIPATA zachitsulo zitseguke zonse mbee!
  • Hymn 106 MZIMU Woyera, mudzetu,
  • Hymn 1645 Nafera inetu, nafera inetu
  • Hymn 726 Mundidzze ndi chikondi,
  • Hymn 234 IMFA ndi mfumu ya mdimawo,
  • Hymn 772 Muwalimbikitse onse
  • Hymn 622 Tiyamikira ‘Tate,
  • Hymn 164 Yendani, Mfumu yamtendere
  • Hymn 218 Mbuye Yesu ndi Atate,
  • Hymn 1176 Sandinyenga, salephera;
  • Hymn 569 Tiimbe ndi kulalikira

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version