Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 102 MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine

  1. Home   »  
  2. Hymn 102 MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine

Hymn 102 MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 102 MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine

 

MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine
E, ngati mvula m’dziko lakuuma,
Ndikhale munda wanu wakupatsa
Zipatso zoyenera Mbuyeyo.

Mphunzitsi, ndinu mudziŵitse ine
Chikondi chanu chija chachikulu;
Lembani mawu anu pamtimanga,
Kuti ndikhumbukire zanuzo.

Wosangalatsa, ine ndikalira
Muchotse nsoni, m’mtimamo mudikhe;
Mundigoneke pachifuwa chake
Cha Yesu kuti ndikakondwepo.

Wotsogolera, munditsogolere
Kuti n’kafike kwawo kwa Atate,
Nditsate Yesu ndikuyendayenda
M’njira yomweyo anapondamo.

Mthandizi ndinu, mndithangate ine
Kupempha bwino izo zindisoŵa.
Kupempha monga Mlungu amafuna
Kulingalira zake zokhazo.

Mzimu Woyera, n’dzipereke ndense,
Mundichitire ntchito yaikulu;
Mtima woyera ndi womvera mpatse,
Wodzala ndi chikondi chanucho.

Post navigation

Previous: Hymn 101 MZIMU Woyera, mudze mumitima mwathumo,
Next: Hymn 103 MPUME pa inetu, Mpweya wa Mulungu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1012 Ndi zipatsozo,
  • Hymn 191 AMBIRI tikondwera mwa Yesu,
  • Hymn 946 Ngakhale enawo aleke kwimbako,
  • Hymn 212 Onse am’Mwamba ali mowemo,
  • Hymn 1332 Imba kawiri ndi kawirinso,
  • Hymn 1137 Masiku ena pali mdima,
  • Hymn 1556 Mzimu Woyera, mudzetu kwa ine,
  • Hymn 1799 Mulungu atipatsa mphamvu
  • Hymn 628 E! chisomo chosaleka
  • Hymn 762 “Ndi thupi lopatsidwali
  • Hymn 1278 Kuti muyeretsa mtima ndibvomeratu;
  • Hymn 93 Mverani mbiri yozizwitsa
  • Hymn 568 Taukani, taonani
  • Hymn 1078 Khalatu woyera
  • Hymn 1079 Khalatu woyera,
  • Hymn 1077 Khalatu woyera,
  • Hymn 945 Tiyeni pamodzi,
  • Hymn 1255 Chitha nchiani kund’yeretsa?
  • Hymn 1 NDINU wakuyera! Wamphamvu zonse.
  • Hymn 640 Anakwatira kale
  • Hymn 12 NDITAMATU Ambuyangayu,
  • Hymn 83 Mpulumutsi Wokondedwa,
  • Hymn 293 LIMBA mtima mbale wanga
  • Hymn 322 Walira Yesu m’dziko linoli,
  • Hymn 1076 Khalatu woyera,
  • Hymn 1408 Kodi mwalandira Yesu?
  • Hymn 1363 Tamani Ambuye,
  • Hymn 393 ZOPEREKA tiperekazi,
  • Hymn 944 Tiyeni nonsenu okonda Yesuyo,
  • Hymn 1313 Zindichulukirazi
  • Hymn 1080 Ambuye mundisunge
  • Hymn 692 Paulendo wathu
  • Hymn 1364 Uzani zamphamvu,
  • Hymn 1362 Mulungu wathu tiyamika,
  • Hymn 1817 Ndi m’munda muja chete, phee!
  • Hymn 971 Ndinu Mbusa wanga;
  • Hymn 18 POKHALA Inu
  • Hymn 1370 Mphepo yay’kulu yakuombayo,
  • Hymn 539 Anafika ‘kazi omwe
  • Hymn 1252 Pakukumbukira zanga
  • Hymn 191 Sindifuna Mbuye wina,
  • Hymn 521 Apunzitsi, ana omwe,
  • Hymn 1443 Ambuye Yesu anatsira
  • Hymn 206 YESU, mulikundipempha
  • Hymn 456 Tizikondana, tisekere
  • Hymn 1361 Ndi Aleluya imbirani
  • Hymn 1472 Ona! Ona! Onatu!
  • Hymn 211 TIDZALAKALAKA kuwonana naye,
  • Hymn 482 TCHIMO musalole, musadziipitse,
  • Hymn 112 Pangano lake m’mwaziwo
  • Hymn 1824 Mulungu wathu Mmodzi yekha
  • Hymn 175 Mlungu mverani, mphamvu patseni,
  • Hymn 213 Mawu a Yesu ati: “Msangatu
  • Hymn 243 KONDWANI nonsenu,
  • Hymn 576 Kondwerani nonsenu
  • Hymn 274 YESU and’itana,
  • Hymn 924 Kodi uli ndi chisoni
  • Hymn 1227 Ndiyamika Mbuye wanga
  • Hymn 1558 Wosangalatsa, ine ndikalira
  • Hymn 810 Tsopano lino kwada bii,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version