Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 375 YESU m’khale nafe

  1. Home   »  
  2. Hymn 375 YESU m’khale nafe

Hymn 375 YESU m’khale nafe

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 375 YESU m’khale nafe

 

YESU m’khale nafe
Nthaŵi yomweyi,
Kuti mphamvu zanu
Tilandirezi.

Mzimu Wakuyera
Mutipatsetu,
Mtima wathu wonse
Usakhale duu.

Moyo watsopano
Ulimbitse ’fe,
Mlungu wathu yemwe
Timdikirabe.

Post navigation

Previous: Hymn 360 KRISTU wakuyeratu,
Next: Hymn 381 MONGA zomera zonsezo

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1359 Ndi Aleluya imbirani
  • Hymn 78 ALINKUDZA wansoni Munthu,
  • Hymn 612 Oyamika Mlungu mbwere,
  • Hymn 197 NDIKHULUPIRA’Nu,
  • Hymn 45 Malawi dziko lokongola,
  • Hymn 177 Tate, ndili mwana wanu,
  • Hymn 490 YESU adza kuwerenga,
  • Hymn 583 Anabadwa,
  • Hymn 1443 Ambuye Yesu anatsira
  • Hymn 371 Mulungu, anthu ‘fe
  • Hymn 1772 Iye amakhutitsa
  • Hymn 1499 Simbanitu mwachete
  • Hymn 306 Ona Mwanawanakhosayo
  • Hymn 297 POKUMANA m’mayesero a dziko lino,
  • Hymn 710 Nthano ya Hananiyayo
  • Hymn 374 Pakuti Mfumuyo
  • Hymn 1741 Yesu munalaswa m’mtima,
  • Hymn 124 PAMTANDAPO, pamtanda,
  • Hymn 346 PEMPHERO ndiko kufuna,
  • Hymn 1738 “Senzani mtanda wanuwo.”
  • Hymn 599 Mlengi wathu Wakuyera,
  • Hymn 8 MITAMBO inu yakumwambako
  • Hymn 1857 Ndinagona mwa zoipa,
  • Hymn 328 Yesu ndiye mphamvu yanga,
  • Hymn 403 NDIYIMBA ndi chimwemwe lero,
  • Hymn 188 Ine ndili ndi manyazi
  • Hymn 474 Yesu ndafikatu,
  • Hymn 409 Yesu adza kuwerenga
  • Hymn 485 POMPANO pandikonda
  • Hymn 82 Mlendo wa Kumwambayo
  • Hymn 893 Mtima wanga ndikonzera,
  • Hymn 844 Pogona ife, amadzuka
  • Hymn 996 Leka zakuipa zako,
  • Hymn 631 Mulungu wa Yakobo Inu, mdyetsa anthu anu,
  • Hymn 1155 Abale angakhale m’talimo
  • Hymn 259 Zoipa zakanikadi,
  • Hymn 1817 Ndi m’munda muja chete, phee!
  • Hymn 54 Dalitsani mafuko onse,
  • Hymn 434 Zondipingitsa zonse
  • Hymn 1560 Mthandizi ndinu, mndithangate ine
  • Hymn 565 Koma sitimpenya m’khola
  • Hymn 474 MPULUMUTSI, Mbusa wathu,
  • Hymn 418 UDINDO wolalikira Uthenga,
  • Hymn 1425 Apempha malo Ambuye;
  • Hymn 269 NDILIRA ine kukayenda
  • Hymn 481 USACHIMWE konse,
  • Hymn 1269 Ndifoka ndi zoipazo,
  • Hymn 200 Ndi tsopano tilindira
  • Hymn 196 NDI inetu sinditha’yi
  • Hymn 884 Mndikumbutse zomwe
  • Hymn 181 Zonse ndinakonda kale
  • Hymn 623 Mbuye, tikuthokozani,
  • Hymn 347 YESU, ndipemphera
  • Hymn 310 MBUYE munditsogolere,
  • Hymn 253 Adzakhala pampandopo
  • Hymn 118 PANALI munthu amene,
  • Hymn 220 Kalekale ndinathawa,
  • Hymn 1026 Inde nditaya chumacho,
  • Hymn 1164 Tikakhulupira
  • Hymn 125 Aliponso mabvuto, ena ndi oipa;

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version