Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 354 ATATE, tifika pamaso panu;

  1. Home   »  
  2. Hymn 354 ATATE, tifika pamaso panu;

Hymn 354 ATATE, tifika pamaso panu;

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 354 ATATE, tifika pamaso panu;

 

ATATE, tifika pamaso panu;
Mukomane ndi ife, Mbuye wathu.

Mitima yathu iyi nayo njanu,
Muiyeretse, muikonze Mbuye.

Ndi maso athu awa nawo nganu,
Muŵapenyetse zinthu zanu zokha.

Ndi manja athu awa nawo nganu,
Agwiretu ntchito yanu yokhayo.

Ndi miyendo yathu iyinso njanu,
Ithamange m’ntchito yanu yokhayo.

Ndi milomo yathu iyinso njanu,
Ilalike Mawu anu kwa onse.

Ndi makutu athu awanso nganu,
Muŵamvetse Mawu anu okhawo.

Tidziperekadi konse kwa Inu
Tikakhale anthu anu okhawo.

Post navigation

Previous: Hymn 353 ATATE Wamkulu ndi Wamphamvu zonse,
Next: Hymn 355 DZIKO lonse mlambire

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 9 Mpingo woyera wa kwa anthuonse
  • Hymn 1077 Khalatu woyera,
  • Hymn 37 YESU analikhanda
  • Hymn 159 Kamwana Yesu ‘nabadwa,
  • Hymn 276 MKRISTU, ulimbike
  • Hymn 4 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 239 TILI ndi mtendere
  • Hymn 543 Kuli kaphiri m’talimo
  • Hymn 225 NDIDZAIMBA za Mulungu,
  • Hymn 1701 Nditani Bwenzi langa
  • Hymn 819 Lero tigone,
  • Hymn 1255 Chitha nchiani kund’yeretsa?
  • Hymn 1790 Imfa ya anthu ake imkomera,
  • Hymn 1422 Abwenzi ‘nu, abwenzi ‘nu,
  • Hymn 1178 Mawu omwewo, nyimbo yomweyi,
  • Hymn 1081 Ndikabisala mwanu
  • Hymn 239 Akumwambawo
  • Hymn 316 NDAMVATU kuti tifika komweko
  • Hymn 1563 Mufike monga nyali younika m’mtimamo,
  • Hymn 594 Monga may’ asusuza
  • Hymn 403 NDIYIMBA ndi chimwemwe lero,
  • Hymn 107 Panalibe mwa abale
  • Hymn 523 “Ndidzawalandira,
  • Hymn 1171 Mulungu wanga
  • Hymn 1747 Yesu aitana ife;
  • Hymn 254 PAMENE ndisawuka,
  • Hymn 1320 Ndayang’anira Mbuyeyo,
  • Hymn 240 Nyama za m’thengo
  • Hymn 429 M’DZANJA lanu Ambuye,
  • Hymn 1559 Wotsogolera, munditsogolere
  • Hymn 232 WAFUNAFUNA ine
  • Hymn 750 Yesu Mbuyathu, Inu nomwe ‘Nu,
  • Hymn 294 POYESEDWA ine
  • Hymn 1460 Akuti anthu akumvera
  • Hymn 1442 Khulupira mawu onse
  • Hymn 1810 Kalelo Mbuye Yesu
  • Hymn 1556 Mzimu Woyera, mudzetu kwa ine,
  • Hymn 1186 Yesu anafa pamtandapo,
  • Hymn 268 Potuluka m’mudzimo
  • Hymn 173 MWAMVA Mawu a Mulungu;
  • Hymn 1729 Munthu Wazisoniyo
  • Hymn 925 Kodi umadandaula:
  • Hymn 1392 Mlungu kuona athiratu
  • Hymn 1264 Chifuniro change, Mbuye, Ndiperekachi;
  • Hymn 298 “Tadodoma, abusa,
  • Hymn 1588 Wandiwombola inetu
  • Hymn 465 Yesu atiuza tiwale pa
  • Hymn 1410 Nthawi zonse mufunabe
  • Hymn 164 WANENA ndi Yesu,
  • Hymn 1767 Ndiye anayang’ana
  • Hymn 486 MPULUMUTSI Yesu,
  • Hymn 217 E! kwa Inu, E! kwa Inu!
  • Hymn 1592 Tsono mubwere inunso,
  • Hymn 369 LERO mwatipatsa moyo,
  • Hymn 1044 Yesu sakusiya konse;
  • Hymn 1093 Odala ndi onsewo
  • Hymn 45 IFE timakufunani
  • Hymn 1444 Wamoyo ndiye Yesudi,
  • Hymn 773 Mtsinje woyerawo
  • Hymn 1040 Ukafuna kulemera,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version