Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 308 AULENDO, munka kuti

  1. Home   »  
  2. Hymn 308 AULENDO, munka kuti

Hymn 308 AULENDO, munka kuti

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 308 AULENDO, munka kuti

 

AULENDO, munka kuti
Ndi zindodo m’manja mwanu?
Paulendo tizipita;
Aitana Mbuye wathu;
Pamapiri, pamadambo
Tizipita komwe kwawo.
Tizipita komwe kwawo
Kuli dzikolo labwino,
Tizipita komwe kwawo
Kuli dzikolo labwino.

Kodi simuopa njira,
Inu anthu akufoka?
Ayi, atiperekeza
Mbuye wathu wotikonda.
Iye amakhala nafe,
Natitsogolera ife.
Atitsogolera ife
Kuli dzikolo labwino.
Atitsogolera ife
Kuli dzikolo labwino.

Mundiuze, aulendo,
Muli chiani m’Mwamba muja?
Atibvekako zoyera
Akorona natininkha;
Moyo, moyo atipatsa,
Kwa Mulungu tidzakhala.
Kwa Mulungu tidzakhala
Kuli dzikolo labwino,
Kwa Mulungu tidzakhala
Kuli dzikolo labwino.

Kodi inu, aulendo,
Ife titsagane nanu?
Inde, mudze inu nonse,
Mudze nafe paulendo.
Inde, mutiperekeze,
Yesu atilinda ife.
Yesu atilinda ife
Kuli dzikolo labwino,
Yesu atilinda ife
Kuli dzikolo labwino.

Post navigation

Previous: Hymn 300 AKRISTU limbikani,
Next: Hymn 321 PAKUONA imfayo

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1245 Ine ndidzakuonetsa
  • Hymn 1269 Ndifoka ndi zoipazo,
  • Hymn 1233 Tsopano ndibukitsabe chikondi chanu chija
  • Hymn 535 Mbuye timlemekeze,
  • Hymn 1040 Ukafuna kulemera,
  • Hymn 1738 “Senzani mtanda wanuwo.”
  • Hymn 276 MKRISTU, ulimbike
  • Hymn 385 Tsopano, poyamba paja,
  • Hymn 1238 M’mene ndifa inedi,
  • Hymn 157 Mbuye, Mzimu Woyera
  • Hymn 927 Pakutsazikana nanu
  • Hymn 152 Inde, Yesu, mundikonda,
  • Hymn 444 YEMWE afesa nalira,
  • Hymn 1225 Ndinachita mphulupulu,
  • Hymn 897 Ndine mlendo pansi pano,
  • Hymn 1852 Mbuye ndamva mwawazira
  • Hymn 1688 Mulibe m’mandamu,
  • Hymn 518 Ana a Yerusalemu
  • Hymn 436 Yesu ndiye Mbusa,
  • Hymn 1395 Mulungu ali nane!
  • Hymn 30 Tamandani Mbuye,
  • Hymn 108 MBUYE wondipulumutsa,
  • Hymn 28 AMBUYE ngwodalitsika,
  • Hymn 830 Atate ndiyamika, mwandisamalira leroli;
  • Hymn 409 ANTHU akum’maŵa
  • Hymn 29 CHIKONDI cha
  • Hymn 43 GETSEMANI, Getsemani,
  • Hymn 361 AMBUYE munapatsa tsiku
  • Hymn 396 PETURO ’nafunsa Hananiya:
  • Hymn 687 Bukitsani mawunso
  • Hymn 1050 Ndafoka inetu,
  • Hymn 486 MPULUMUTSI Yesu,
  • Hymn 1005 Mdani adza nazo mphamvu,
  • Hymn 129 WODALA ndiye munthuyo,
  • Hymn 352 Tiyamike Mlunguyo,
  • Hymn 10 Kristu Mfumuyo yaulemerero!
  • Hymn 891 Akakusowa malo
  • Hymn 1128 Mbuyanga Yesu, mundisunge ine
  • Hymn 233 M’mene ndapenya mwazi wa
  • Hymn 1170 Pamtanda wake
  • Hymn 1088 Mndiyandikitse nanu, Yesu,
  • Hymn 489 YESU ndiye Bwenzi lathu,
  • Hymn 561 Uyu ‘natsikira kuno,
  • Hymn 1274 Chisoni andichotsera Mbuyeyu,
  • Hymn 46 O! ufulu tigwirizane
  • Hymn 546 Kulibe wokwanira ‘yi
  • Hymn 524 Wokoma Mbuyathu
  • Hymn 1724 Ambuye mthandize inetu
  • Hymn 1526 Mbuye wondipulumutsa
  • Hymn 30 YEHOVA, Mbusa wangadi,
  • Hymn 1733 Adzabwera Iyenso
  • Hymn 1334 Walandira inetu
  • Hymn 291 Ndi milomo yathu iyinso njanu,
  • Hymn 1823 Opani Iye, nimuleke
  • Hymn 1347 Akukonda, akukonda,
  • Hymn 1538 Mzimu Woyera, mudzetu
  • Hymn 358 Dzina lake Yesuyo,
  • Hymn 548 Kale anthu m’kholamo
  • Hymn 370 Pakuti Mbuye Mlunguyo
  • Hymn 1311 Pothawira pena ‘yi,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version