Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 194 AMBUYE’naitan’ne;

  1. Home   »  
  2. Hymn 194 AMBUYE’naitan’ne;

Hymn 194 AMBUYE’naitan’ne;

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 194 AMBUYE’naitan’ne;

 

AMBUYE’naitan’ne;
“Dzapumulire kuno,
Tsamira mutu, mwana’we
M’chifuwa mwanga muno.”

Ndabwera kwa Ambuyeyo;
Wolema, wachisoni;
Anandipulumutsako,
Nakondweretsa ine.

Ambuye naitana’ne;
“Ndipatsa anthu madzi,
Wotopa ndi waludzu’we
Dzamwere moyo kuno.”

Ndabwera kwa Ambuyeyo.
Ndamwera madzi awa;
Laleka ndithu ludzulo,
Tsopano moyo wadza

Ambuye naitana’ne;
“La dziko ndine Dzuŵa,
Yang’ana Ine, kwacha’we,
Wachoka mdima uja.”

Ndayang’anira Mbuyeyo
Ndzapeza Dzuŵa langa
Londiyendetsa bwinoli
Pa njira yanga yonse.

Post navigation

Previous: Hymn 193 THANTHWE long’ambikatu,
Next: Hymn 195 YESU wondikondadi,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 756 Sindili woyenera ‘ne,
  • Hymn 336 KULINSO dziko lowala M’mwamba,
  • Hymn 681 Ankhondo a Mulungu ‘nu, yendani m’njiramo,
  • Hymn 1474 Zilepheradi zonse kugula moyowo,
  • Hymn 157 INU nonse ovutidwa,
  • Hymn 1627 Adzabwera, adzabwera;
  • Hymn 1553 Mpume pa inetu, Mpweya wa Mulungu,
  • Hymn 223 Ndafoka, ndaipa,
  • Hymn 50 Akhristu nyamulani
  • Hymn 744 Kristu ndi mwini moyo wathuwu,
  • Hymn 58 PAMTANDAPO Ambuyeyo
  • Hymn 769 Ndi kutsukidwa m’mwazimo
  • Hymn 1121 Ndifuna Yesuyo,
  • Hymn 37 Pozunzidwa inu ponseponsepo
  • Hymn 1052 Ndilira mtima wotamanda
  • Hymn 1730 Anapeputsidwako,
  • Hymn 970 Pena kumwa nawo,
  • Hymn 665 Pomangidwa anthu nayo
  • Hymn 1310 Yesu wondikondadi,
  • Hymn 363 Funani Mlungu tsopano,
  • Hymn 1055 E, mtima watsopano ndi
  • Hymn 354 ATATE, tifika pamaso panu;
  • Hymn 1564 Mufike monga moto wakuotcha zomwezo.
  • Hymn 1843 Chigwa choopsacho cha imfa ndikachilowera,
  • Hymn 183 Mlemekeze, bukitsani,
  • Hymn 594 Monga may’ asusuza
  • Hymn 1020 Ngati umtsata Mpulumutsi wakoyo,
  • Hymn 872 Mtidzutse, Mbuyetu,
  • Hymn 793 Tikondwera kuti
  • Hymn 483 NTHAŴI yaubwana yatha,
  • Hymn 1249 Tsirizani ntchito yanu
  • Hymn 200 Ndi tsopano tilindira
  • Hymn 468 Ife tikondana nanu,
  • Hymn 1516 Pakudera nkhawa ‘ne,
  • Hymn 1001 Mafumu atiuza tikaletse ukapolo,
  • Hymn 1758 Poti Mulungu wathu
  • Hymn 407 Zochimwa sizilowako,
  • Hymn 91 NDITAME Mlungu m’mtimamo,
  • Hymn 194 Kuli dziko labwino m’Mwamba
  • Hymn 9 TAMANI Ambuye,
  • Hymn 739 Ndilibe wondithangata ‘ne ‘yi,
  • Hymn 1264 Chifuniro change, Mbuye, Ndiperekachi;
  • Hymn 153 NDAKUMANA ndi bwenzi lokomalo,
  • Hymn 648 Mulungu wa Kumwamba,
  • Hymn 58 Titasokera tinabwerera,
  • Hymn 1749 Chifukwa chipulumutso
  • Hymn 834 Tiyamike Mlungu wotipatsa zachifundozi,
  • Hymn 668 Achisoni, obvutidwa,
  • Hymn 499 ‘Nafera Mbuye wanga
  • Hymn 440 ZIKOMO Ambuye wathu,
  • Hymn 1625 Ife tonse tikumbuke
  • Hymn 466 OSANATU, osana,
  • Hymn 577 Adagona m’ndyeromo
  • Hymn 694 Sadalekeza kuyamika
  • Hymn 359 TADZUKA mzimu wanga ‘we,
  • Hymn 1183 Adalitsika, indetu,
  • Hymn 416 Woyenera ndani kunka
  • Hymn 565 Koma sitimpenya m’khola
  • Hymn 1646 M’busa wokoma ndi Mbuyangayo,
  • Hymn 1128 Mbuyanga Yesu, mundisunge ine

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version