Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 128 ANTHU m’maiko onse

  1. Home   »  
  2. Hymn 128 ANTHU m’maiko onse

Hymn 128 ANTHU m’maiko onse

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 128 ANTHU m’maiko onse

 

ANTHU m’maiko onse
Akhala mitundu;
Kapena m’dziko lino
Akhala anzathu;
Agona mwa zoipa,
Apulukiradi,

Ati, Mutilangize
Abale, bwerani.

Ngakhale alemera
Ndi chuma cha dziko,
Kodi akakondwera
Opanda Mulungu?
Kodi akhala mwaŵi
Otsata zawozo?
Iyai, awonongeka,
Apeza tsokalo.

Ndi ife akudziŵa
Chikondi cha Mlungu,
Kodi tidzaŵamana
Kuŵala kwa Kristu?
Chipulumutso! Inde,
Tichibukitsetu,
Kuti mitundu yonse
Ibwere kwa Yesu.

Akristu nyamulani
Maneno a Mulunguyo,
Ndi moyo lalikani
Pa dziko lonselo;
Ndi Yesu Mpulumutsi
Anatiferatu;
Adzabvomera onse;
Ndi Mwana wa Mlungu.

Post navigation

Previous: Hymn 120 MUNDINYEMERE ’ne
Next: Hymn 141 TAONANI pamtandapo,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 949 Mundiwalire m’njira mwangamo,
  • Hymn 1811 Tipulumuka mommo,
  • Hymn 293 Tidziperekadi konse kwa Inu
  • Hymn 664 Komwe asauka anthu
  • Hymn 876 Mtidzutse, Mbuyetu,
  • Hymn 711 Ife tonse tichenjere
  • Hymn 243 Mtima wanga udzakondwera,
  • Hymn 1847 Ife tonse, ife tonse,
  • Hymn 97 Maso ndi maso ndi Kristu,
  • Hymn 194 Kuli dziko labwino m’Mwamba
  • Hymn 142 Kukondwa kwa wodwalayo
  • Hymn 1306 Ndi ine ndasaukadi,
  • Hymn 1774 Poti akumbukira
  • Hymn 1311 Pothawira pena ‘yi,
  • Hymn 109 MUTHIRE, Yesu, m’mtimanga
  • Hymn 881 Tili nazo zotiyesa,
  • Hymn 1586 Mbuye Yesu timtamanda
  • Hymn 57 Ife tiyembekezera Yesu,
  • Hymn 153 Pemphero ndiko kufuna,
  • Hymn 1761 Amithenga anaimba
  • Hymn 223 ATI Yesu Mbuyeyo:
  • Hymn 1197 Ndafoka ine kale,
  • Hymn 45 IFE timakufunani
  • Hymn 1272 Muyambe ntchito yanuyi,
  • Hymn 310 Tafika kwa inu mutiunikire,
  • Hymn 87 IDZANI nonse ’nu
  • Hymn 849 Tadzuka mzimu wanga’we
  • Hymn 307 ABALE anga ine ndikupita,
  • Hymn 461 ANA inu, myamikeni
  • Hymn 348 Aitana,
  • Hymn 1819 Pokondwa ndi poona bvuto
  • Hymn 1170 Pamtanda wake
  • Hymn 733 Ndimamva ludzu Yesu,
  • Hymn 319 Koma zina sizinadziwa ayi,
  • Hymn 886 Chikondi, chimwemwe,
  • Hymn 1423 Oipa inu nonsetu,
  • Hymn 1584 Konda dzinalo la Yesu
  • Hymn 410 Ana ake angonga
  • Hymn 1192 Pamtanda woopsa
  • Hymn 875 Mtidzutse, Mbuyetu,
  • Hymn 1640 Alinkudza Ambuye Yesu
  • Hymn 569 Tiimbe ndi kulalikira
  • Hymn 1418 Khulupirani kuti mukalowe m’Mwambamo,
  • Hymn 1581 Ndi nyimbo yabwino
  • Hymn 231 AMBUYE, m’imfamo
  • Hymn 64 LERO Kristu anauka,
  • Hymn 1163 Tili ndi mtendere
  • Hymn 221 Yesu and’itana,
  • Hymn 972 Akristu limbikani,
  • Hymn 77 MMENE Yesu adzabwera,
  • Hymn 64 Mantha, nkhawa, ndi chisoni
  • Hymn 262 Tumphatumpha moyo wanga,
  • Hymn 721 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 360 KRISTU wakuyeratu,
  • Hymn 410 MAWU akewo anamveka ponse,
  • Hymn 1189 Ambuye Mulungu,
  • Hymn 20 CHIKONDI cha Mulungu wathu,
  • Hymn 1432 Lero lino m’bale wanga,
  • Hymn 411 Yesu adza kukundika
  • Hymn 375 YESU m’khale nafe

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version