Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 113 KALERO anthu onse

  1. Home   »  
  2. Hymn 113 KALERO anthu onse

Hymn 113 KALERO anthu onse

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 113 KALERO anthu onse

 

KALERO anthu onse
Nachimwa kwa Mulungu
Mulungu anawona
Nawona tchimo lawo,
Nafuna kwawononga,
Nafuna kwawononga.

Mulungu anatuma,
Natuma mvula ija,
Nadzaza dziko lonse
Anafa anthu onse,
Anafa m’mvula muja,
Anafa m’mvula muja.

Mulungu anatuma,
Natuma Nowa uja,
Wamanga chombo chake,
Ndi chachitalitali,
Nowayo nayendamo,
Nowayo nayendamo.

Nowayo anatuma,
Natuma chikwangwala,
Chatsika pansi pansi,
Chosabwerera konse,
Chithaŵa m’talitali,
Chithaŵa m’talitali.

Kutuma wabwereza,
Natuma nkhunda ija,
Yatsika pamadzipo,
Yathyolatu mayani,
Yampatsa Nowa yemwe,
Yampatsa Nowa yemwe.

Kalelo Mbuye Yesu
’Nafera anthu onse,
Ndiyeyo chombo chathu,
Tikabisala mommo
Tipulumuka mommo,
Tipulumuka mommo.

Post navigation

Previous: Hymn 112 ELISA mneneri,
Next: Hymn 114 NDIPO Eliya anati kwa Elisa:

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1089 Ndionetsere kuunika
  • Hymn 1856 Mzimu, msandipitirire,
  • Hymn 305 NDALIMVA dziko la m’talimo,
  • Hymn 604 ‘Tate, Mwana, Mzimu, ndinu
  • Hymn 1116 Kwawo kwa Mbuyako
  • Hymn 1743 M’kati mwa zobvuta zathu
  • Hymn 124 PAMTANDAPO, pamtanda,
  • Hymn 319 NDIDZATANI ine,
  • Hymn 1805 Anafa m’mvula muja
  • Hymn 1077 Khalatu woyera,
  • Hymn 705 Tikhaletu nawo, Mbuye,
  • Hymn 1778 Angelo kwezani
  • Hymn 656 Ndipumulire panupo,
  • Hymn 498 Yesu akonda,
  • Hymn 2 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 412 Kudzachera tsiku lijalo
  • Hymn 927 Pakutsazikana nanu
  • Hymn 228 Ataya zoipa,
  • Hymn 1562 Mzimu Woyera, mudze mumitima mwathumo,
  • Hymn 750 Yesu Mbuyathu, Inu nomwe ‘Nu,
  • Hymn 1462 Dzina la Yesu ndi lokoma,
  • Hymn 866 Pa la Mulungu tibwera kulandira zidazo;
  • Hymn 204 Kumandako, kumanda
  • Hymn 65 Chisomo chodabwitsacho
  • Hymn 1657 Mbuye, mutsaganebe
  • Hymn 1310 Yesu wondikondadi,
  • Hymn 1307 Ndi ine simufuna ‘yi
  • Hymn 132 MVERA mtima wanga ’we
  • Hymn 1539 Kudzoza kwa Kumwambako
  • Hymn 1611 Nadzuka m’mandamo
  • Hymn 236 NDIDZIWITSITSA
  • Hymn 78 Ndipereka zanga zonse,
  • Hymn 1723 Unakhetsedwa mwazi do!
  • Hymn 358 MLUNGU ali muno,
  • Hymn 1815 Choposa nalo thupilo,
  • Hymn 418 UDINDO wolalikira Uthenga,
  • Hymn 1635 Pakwitana Mbuye wanga,
  • Hymn 76 E, MOYO wanga’we
  • Hymn 1279 Kuti munditsogolera paulendopo;
  • Hymn 1083 “Khala mwa Ine,” Yesu anatero;
  • Hymn 728 A! Yesu, ndapangana
  • Hymn 457 KALE m’mzinda wachifumu
  • Hymn 344 M’watame,
  • Hymn 398 KODI mbale wasimba zachikhululukiro,
  • Hymn 993 Pakumalizidwa
  • Hymn 618 ‘Dzani Mbuye msangatu,
  • Hymn 8 Nanu Atumwi akumveka aja,
  • Hymn 533 Ananu, ziimbani,
  • Hymn 193 A! Kumwamba
  • Hymn 1428 Penyetsetsa Yesu
  • Hymn 394 TATENGA mphatso zotani?
  • Hymn 474 Yesu ndafikatu,
  • Hymn 41 Tiyeni, tiyeni,
  • Hymn 1125 Ndifuna Inu, Yesu,
  • Hymn 77 MMENE Yesu adzabwera,
  • Hymn 311 Tifuna kuchita chifuniro chanu,
  • Hymn 920 Yatha misoziyo,
  • Hymn 1669 Ukafuna kumdziwitsa,
  • Hymn 189 Koma Iye wandipeza;
  • Hymn 298 “Tadodoma, abusa,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version