Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 102 MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine

  1. Home   »  
  2. Hymn 102 MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine

Hymn 102 MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 102 MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine

 

MZIMU Woyera, mudzetu kwa ine
E, ngati mvula m’dziko lakuuma,
Ndikhale munda wanu wakupatsa
Zipatso zoyenera Mbuyeyo.

Mphunzitsi, ndinu mudziŵitse ine
Chikondi chanu chija chachikulu;
Lembani mawu anu pamtimanga,
Kuti ndikhumbukire zanuzo.

Wosangalatsa, ine ndikalira
Muchotse nsoni, m’mtimamo mudikhe;
Mundigoneke pachifuwa chake
Cha Yesu kuti ndikakondwepo.

Wotsogolera, munditsogolere
Kuti n’kafike kwawo kwa Atate,
Nditsate Yesu ndikuyendayenda
M’njira yomweyo anapondamo.

Mthandizi ndinu, mndithangate ine
Kupempha bwino izo zindisoŵa.
Kupempha monga Mlungu amafuna
Kulingalira zake zokhazo.

Mzimu Woyera, n’dzipereke ndense,
Mundichitire ntchito yaikulu;
Mtima woyera ndi womvera mpatse,
Wodzala ndi chikondi chanucho.

Post navigation

Previous: Hymn 100 MUBWERE Mzimu Wakuyera,
Next: Hymn 121 MULUNGU, anthu ’fe

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 473 Mzinda woyerawo!
  • Hymn 1764 Yesu ndinu Mbuye wathu,
  • Hymn 1168 Aleluya, muyenera!
  • Hymn 538 Iye anachoka kwawo,
  • Hymn 1730 Anapeputsidwako,
  • Hymn 373 NYUMBA ya Mulungu, ili pano,
  • Hymn 51 PANTHAWI yakufa Ambuye,
  • Hymn 637 Mbuyathu wokondedwa,
  • Hymn 342 Ambiri,
  • Hymn 880 Bwenzi lathu ndiye Yesu
  • Hymn 1821 Angelo amazinga nyumba
  • Hymn 1085 “Khala mwa Ine,” ndinu mwini mphamvu,
  • Hymn 576 Kondwerani nonsenu
  • Hymn 716 Tibwezeretu bwanjiko?
  • Hymn 893 Mtima wanga ndikonzera,
  • Hymn 302 NDIDZE pafupi pa
  • Hymn 436 Yesu ndiye Mbusa,
  • Hymn 872 Mtidzutse, Mbuyetu,
  • Hymn 596 Mlungu ali nane;
  • Hymn 1105 Khala chete mtima wanga
  • Hymn 1658 Idza wolema,
  • Hymn 220 MULUNGU mundichitire chifundo,
  • Hymn 1154 Zakutsogolo sitidziwa ‘yi;
  • Hymn 1327 Bwezatu, bwezatu,
  • Hymn 1459 Ambuye mulowetse
  • Hymn 1233 Tsopano ndibukitsabe chikondi chanu chija
  • Hymn 1354 Mzimu Woyera, m’mtimamo
  • Hymn 788 Moyo watsopano
  • Hymn 743 Mudze, anthuni, talawani ‘nu
  • Hymn 684 Zipata zatsegudwa mbee! Za m’dziko monsemo;
  • Hymn 1268 Mundilandiretu,
  • Hymn 30 YEHOVA, Mbusa wangadi,
  • Hymn 394 TATENGA mphatso zotani?
  • Hymn 1392 Mlungu kuona athiratu
  • Hymn 380 ATATE, muwapenya
  • Hymn 1386 Ndi chifundo atipenya
  • Hymn 1771 Iye natsitsa kunsi
  • Hymn 602 Mpulumutsi wakukoma,
  • Hymn 1494 Mbiri yakalelomwe,
  • Hymn 422 DZIKO lonse lapansi,
  • Hymn 1830 Ndiye M’busa wanga
  • Hymn 539 Anafika ‘kazi omwe
  • Hymn 212 Onse am’Mwamba ali mowemo,
  • Hymn 444 YEMWE afesa nalira,
  • Hymn 1389 Tithawire kwa Mulungu,
  • Hymn 792 Dzuwa la Mulungu
  • Hymn 1836 Ndi wamwayi munthu uja
  • Hymn 1111 Pamene ndilemedwa
  • Hymn 236 NDIDZIWITSITSA
  • Hymn 1548 Mtitsitsimutse ife
  • Hymn 1296 Chionerere mwaziwo
  • Hymn 701 Inu Atatuwo,
  • Hymn 375 Zipatso zakezi
  • Hymn 787 Mzimu Wakuyera
  • Hymn 918 Ntchito yonse yakeyo
  • Hymn 1705 Pa Iye padzapo
  • Hymn 1843 Chigwa choopsacho cha imfa ndikachilowera,
  • Hymn 1766 Ndilikulemekeza
  • Hymn 495 Wonga Inu ndikhaledi,
  • Hymn 342 BWENZI lathu ndiye Yesu,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version