Hymn 870 Satana apambana tikayamba kusiyana; December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 870 Satana apambana tikayamba kusiyana; Satana apambana tikayamba kusiyana; Tikayanjana, yemwe adzagonja ndi kuthawa; Mbuyathu adzamthyola konse ndi kumlamulira. Tiyeni tonse, m’Mpingo ‘modzi tiziyenderana.