Hymn 870 Satana apambana tikayamba kusiyana; treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 870 Satana apambana tikayamba kusiyana; Satana apambana tikayamba kusiyana; Tikayanjana, yemwe adzagonja ndi kuthawa; Mbuyathu adzamthyola konse ndi kumlamulira. Tiyeni tonse, m’Mpingo ‘modzi tiziyenderana.