Hymn 1555 Mpume pa inetu, Mpweya wa Mulungu, December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1555 Mpume pa inetu, Mpweya wa Mulungu, Mpume pa inetu, Mpweya wa Mulungu, Kuti inedi ndisafe ‘yitu, Koma ndikhale nanu m’moyo womwe Wangwiro ndi wa nthawi zonsetu.