Hymn 1362 Mulungu wathu tiyamika, December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1362 Mulungu wathu tiyamika, Mulungu wathu tiyamika, ‘Tate, Mwana, Mzimu yemwe Aleluya Inu. Woyera Inu ndi wamphamvu, Muyenera anthu onse Agwadire Inu.