Hymn 1362 Mulungu wathu tiyamika, treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1362 Mulungu wathu tiyamika, Mulungu wathu tiyamika, ‘Tate, Mwana, Mzimu yemwe Aleluya Inu. Woyera Inu ndi wamphamvu, Muyenera anthu onse Agwadire Inu.