Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1173 Sindinanyengedwa konse
Sindinanyengedwa konse
Pakutsata Yesuyo;
Yesu apambana zonse
Ndinalingalirazo.
Pakuyenderana naye
Ndimamdziwa ndi woona;
Ndifunitsa anthu onse
Adziwenso Yesuyo!
Ndifunitsa anthu onse
Adziwenso Yesuyo!