Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 71 DZIKO lino lapansi, ndilibetu abwenzi,

  1. Home   »  
  2. Hymn 71 DZIKO lino lapansi, ndilibetu abwenzi,

Hymn 71 DZIKO lino lapansi, ndilibetu abwenzi,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 71 DZIKO lino lapansi, ndilibetu abwenzi,

 

DZIKO lino lapansi, ndilibetu abwenzi,
Ndili ndekha mpanjira n’kwaŵenitu;
Ndilibetu chakudya, ndilibetu chakumwa,
Ndingoyenda mpanjira n’kwaŵenitu.

N’kwawenitu,
N’kwawenitu,
Dziko lino sikwathu
N’kwaŵenitu.

Dziko lino lapansi mavuto ndi osatha,
Ine sindingalithe n’kwaŵenitu;
Ukasowa chumacho, abwenzi akuthawa,
Koma kwathu satero n’kwaŵenitu.

Anyamata, ‘sungwana
Samaopa Mulungu,
Sichifukwa chinanso n’kwaŵenitu;
Abambo ndi amayi
Samaopa Mulungu,
Sichifukwa chinanso n’kwaŵenitu.

Tiyeni abale ‘fe tiyang’ane kwa Yesu,
Yemwe angatipatse moyowotu;
Moyo uno wam’dziko abale ndi wozunza,
Moyo wokoma ndiwo wa Yesuyo.

Post navigation

Previous: Hymn 70 LAMBIRA, Mfumuyo,
Next: Hymn 72 YESU wakukoma mtima,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 966 Kodi inu, aulendo,
  • Hymn 435 Yesu ndiye Mbusa,
  • Hymn 288 HAYA! ’nzanga taonani
  • Hymn 483 Ndife akuchoka,
  • Hymn 664 Komwe asauka anthu
  • Hymn 357 Yesu ndiye Mtetezi,
  • Hymn 1244 Nthawi ilikudza yonse
  • Hymn 1258 Zonse zina sizikwana,
  • Hymn 466 OSANATU, osana,
  • Hymn 1506 Ndikamfunafuna Iye,
  • Hymn 378 Ku madzi ake odikha
  • Hymn 615 Yamikani nonse ‘nu,
  • Hymn 184 LEKANI kubvutika ndi zinthu za padziko,
  • Hymn 1207 Poyambapo ndakondwadi,
  • Hymn 1035 Mphamvu zathu zonse
  • Hymn 881 Tili nazo zotiyesa,
  • Hymn 1542 Titamire nthawi zonse
  • Hymn 483 NTHAŴI yaubwana yatha,
  • Hymn 1333 Idzatu kwa Yesuyo,
  • Hymn 1586 Mbuye Yesu timtamanda
  • Hymn 683 Musamaopa kanthu ‘yi, tamani Yesuyo;
  • Hymn 891 Akakusowa malo
  • Hymn 370 KWACHA lero kwati mbee,
  • Hymn 353 Anatuma Mtetezi,
  • Hymn 1268 Mundilandiretu,
  • Hymn 818 Mkhululukire,
  • Hymn 1447 Yesu ngwachifundodi,
  • Hymn 883 Pokupempherani
  • Hymn 285 DZIKO lino lapansi,
  • Hymn 1549 Mtitsutse titachimwa
  • Hymn 494 Yesu, E, ndikufunani,
  • Hymn 1110 Mulungu wanga,
  • Hymn 1195 Wafunafuna ine
  • Hymn 402 BWERANITU, bweranitu,
  • Hymn 1455 Uthenga wa Mulungu
  • Hymn 94 KHAMULO liliko
  • Hymn 169 M’manda nagonamo
  • Hymn 1036 Mtima wakufatsa
  • Hymn 311 Tifuna kuchita chifuniro chanu,
  • Hymn 348 Aitana,
  • Hymn 120 MUNDINYEMERE ’ne
  • Hymn 1725 Zochimwa zanga zonsezo
  • Hymn 1274 Chisoni andichotsera Mbuyeyu,
  • Hymn 67 PAMENEPO pokhala madzulo,
  • Hymn 1205 Ndikonda chifukwa
  • Hymn 117 Atate wondipatsazo,
  • Hymn 1678 Yesu nkana saoneka, Aleluya,
  • Hymn 1087 “Khala mwa Ine,” Mbuye, ndifunitsa;
  • Hymn 185 Kondwani nonsenu,
  • Hymn 1045 Ambuye, ndifuna nditsukenitu;
  • Hymn 1017 Tisasungaluke ‘yi,
  • Hymn 413 Yesu ndiye Bwenzi lathu,
  • Hymn 132 Ganizansoni, ali pano,
  • Hymn 924 Kodi uli ndi chisoni
  • Hymn 30 Tamandani Mbuye,
  • Hymn 955 Komwe ndi chimwemwe ine
  • Hymn 217 E! kwa Inu, E! kwa Inu!
  • Hymn 1841 Kumadzi kuli njiratu andiyendetsa bwino,
  • Hymn 261 Munafera pa mtanda
  • Hymn 589 Koma ineyu

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version