Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 23 TIIMBE nyimbo zotamanda

  1. Home   »  
  2. Hymn 23 TIIMBE nyimbo zotamanda

Hymn 23 TIIMBE nyimbo zotamanda

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 23 TIIMBE nyimbo zotamanda

 

TIIMBE nyimbo zotamanda
Mulungu wathu wabwino,
Pakuti akondana nawo
Anthu okhala padziko;
Tero natuma Mwana wake,
Wakukondedwa kalelo,
Kutiphunzitsa ife tonse
Za chikondano chakecho.

Mulungu ndiye wachifundo,
Nadzalandira onsewa
Akuulula mphulupulu
Ndi kukondana ndi Yesu
Tilondelonde njira yake
Yopapatiza yaing’ono;
Adzatilondolera ndiye
Kutifikitsa m’Mwambamo.

Pakuwoloka mtsinje wa imfa
Dzanja Mbuyathu agwira;
Tikadagwira ntchito zake
Atipatsatu korona;
Komwe kulibe masauko,
Pena misozi maliro;
Mulungu tidzamtamandira,
Inde kosalekezanso.

Post navigation

Previous: Hymn 22 MU ZONSE abale yamikani,
Next: Hymn 24 TITAME Mlungu Wakumwamba,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 764 “Chikho cha mwazi wangachi
  • Hymn 269 Atate ‘nu, amayi ‘nu, nonsenu,
  • Hymn 1323 M’manja mopanda kanthu,
  • Hymn 322 PAKUYITANIDWA munthu pa dziko ino,
  • Hymn 1318 Ndibwera kwa Ambuyeyo,
  • Hymn 161 LERO lino mbale wanga,
  • Hymn 1744 Kale ophunzira ake
  • Hymn 1042 Zonse umazinyadira
  • Hymn 1583 Dzina la Yesuyo
  • Hymn 74 Ndipereka zanga zonse
  • Hymn 1310 Yesu wondikondadi,
  • Hymn 996 Leka zakuipa zako,
  • Hymn 925 Kodi umadandaula:
  • Hymn 81 MBUYE Yesu adzabwera,
  • Hymn 201 Ngati zakuipa zathu
  • Hymn 478 YESU atiuza tiŵale ’fe.
  • Hymn 1408 Kodi mwalandira Yesu?
  • Hymn 332 NDIKONDWA kuganizirabe
  • Hymn 904 Komweko akhala Yesuyo
  • Hymn 526 Mnandidzera, Ambuye,
  • Hymn 91 Ufuna kuyera kopambana?
  • Hymn 1810 Kalelo Mbuye Yesu
  • Hymn 979 Limbikani inu nonse,
  • Hymn 1796 Ndikhulupira mwa Ambuye
  • Hymn 813 Wopulumutsa, Inunso
  • Hymn 1438 Yesu akukonda,
  • Hymn 1598 Mtiphunzitse, Mbuye Yesu,
  • Hymn 403 NDIYIMBA ndi chimwemwe lero,
  • Hymn 384 Mulungu akhale nawo
  • Hymn 1097 Njira yanga sindidziwa,
  • Hymn 341 Ayenda,
  • Hymn 1191 Ambuyanga Yesu
  • Hymn 522 Akazi anadza
  • Hymn 557 Usikuwo woyerawo!
  • Hymn 15 YEHOVA ndiye Mbusa wanga,
  • Hymn 1642 M’khola mwa ng’ombe ku Betelehemu
  • Hymn 1766 Ndilikulemekeza
  • Hymn 494 Yesu, E, ndikufunani,
  • Hymn 1458 Satana ndi unyolo
  • Hymn 963 Aulendo, munka kuti
  • Hymn 1685 Nla Mlungu dzuwali;
  • Hymn 400 ONA Mwana wa Nkhosa,
  • Hymn 1712 E! Yesu Mbuye wangadi,
  • Hymn 1483 Pakupempha ife pano,
  • Hymn 747 Tadzanitu, okhulupiradi,
  • Hymn 1792 Mulungu ndiye wachifundo,
  • Hymn 1103 Ndakudani, mnandikonda
  • Hymn 1032 Ntchito za Yesu gwira
  • Hymn 1804 Mulungu anatuma,
  • Hymn 1622 Anthu onse amlambire
  • Hymn 1188 Akumangidwa ndi mzimuwo,
  • Hymn 276 MKRISTU, ulimbike
  • Hymn 160 Kamwana kaja ‘nayamba
  • Hymn 906 Mulibe zoipa m’Dzikolo,
  • Hymn 378 KWEZANI mitu yanuyo,
  • Hymn 177 Tate, ndili mwana wanu,
  • Hymn 1266 E, chimwemwe chachikulu, N’taperekadi
  • Hymn 752 Chakudya chakumwambachi
  • Hymn 848 Mudze, mlowe m’mtimamu,
  • Hymn 275 Mlungu akuyang’aniredi,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version