Chichewa Christian Hymns
Hymn 400 ONA Mwana wa Nkhosa,
ONA Mwana wa Nkhosa,
Ona Mwana wa Nkhosa:
Ona Mwana wa Nkhosa,
Ona Mwana wa Nkhosa.
Malipiro a tchimo,
Ndi imfa yosathayo;
Malipiro a tchimo,
Ndi imfa yosathayo.
Ubadwe mwatsopano,
Ubadwe mwatsopano;
Ubadwe mwatsopano,
Mwa Yesu Ambuyeyo.
Konzeka mbale wanga,
Kukumana ndi Yesu;
Konzeka mbale wanga,
Kukumana ndi Yesu.