Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 397 MBUYE wathu, mutipatsa

  1. Home   »  
  2. Hymn 397 MBUYE wathu, mutipatsa

Hymn 397 MBUYE wathu, mutipatsa

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 397 MBUYE wathu, mutipatsa

 

MBUYE wathu, mutipatsa
Zonse tili nazozo,
Mutikomeratu mtima
Osaleka konseko,
Mutikonda, mutisunga,
Mutisamalira ’fe.

Dzuŵa, madzi, kudya, mpweya,
Moyo, zonse nzanuzi,
Si za ife, nzaulere,
Tingozilandiradi;
Zifumira kwa Aate
Wotikondakondatu.

Monga tilandira, Mbuye,
Mtiphunzitse tonsefe
Tipere chuma chathu
Ndi kusangalalatu;
Zakukhala m’manja mwathu
Tiziyese nzanudi.

Tikhaletu nawo, Mbuye,
Mtima wosauma ’yi
Ndi wofatsa ndi wabwino
Ndi woyerayeradi,
Kuti tiyenere Dzina
La Mbuyathu Yesuyo.

Tisaiwalire ’bale
Athu osadziŵa ’Nu,
Akulira ndi odwala
Tiŵapemphereratu;
Titsanzenso Mbuye Yesu
Ndi k’ŵathangatira ’wo.

Dalitseni, Mbuye, zonse
Zomwe taperekazi,
Mzilandire, nsembe yathu,
Mziyeretse Inudi
Ndi mitima yathu yonse
Tikuyamikirani.

Post navigation

Previous: Hymn 396 PETURO ’nafunsa Hananiya:
Next: Hymn 398 KODI mbale wasimba zachikhululukiro,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 983 Nkhondo ya Satana
  • Hymn 292 Ndi makutu athu awanso nganu,
  • Hymn 1293 Chitsimecho cha mwaziwo
  • Hymn 588 Mlungu, Inutu,
  • Hymn 48 Ngakhale alemera
  • Hymn 857 Mlungu amaunikira
  • Hymn 908 Ndikonda kuganizirabe
  • Hymn 1032 Ntchito za Yesu gwira
  • Hymn 1662 Msandipitire, Yesu,
  • Hymn 1810 Kalelo Mbuye Yesu
  • Hymn 496 MBUYE dalitsani Afirika.
  • Hymn 428 MBUYE mtsitsimutse
  • Hymn 1088 Mndiyandikitse nanu, Yesu,
  • Hymn 1308 Ndi ine, m’mtima Mwanu mbee!
  • Hymn 482 TCHIMO musalole, musadziipitse,
  • Hymn 39 Poyang’ana ena ndi ndalamatu,
  • Hymn 113 KALERO anthu onse
  • Hymn 352 Tiyamike Mlunguyo,
  • Hymn 237 Munasiyatu
  • Hymn 445 TILIMALIMA m’minda,
  • Hymn 236 NDIDZIWITSITSA
  • Hymn 1763 Amithenga anaimba
  • Hymn 270 NDILIRA mtima wotamanda
  • Hymn 303 MEMA nkhondoyo, wadza mdaniyo,
  • Hymn 689 Anapeza Mwana
  • Hymn 1398 Nditama mphamvu yake
  • Hymn 1559 Wotsogolera, munditsogolere
  • Hymn 1346 Ndaima pano, ndaima pakhomo:Lowa, lowa, lowa, lowa!
  • Hymn 1095 Mumtima wakufatsa
  • Hymn 1602 M’mawu a Yesu Mbuyeyo,
  • Hymn 204 Kumandako, kumanda
  • Hymn 1688 Mulibe m’mandamu,
  • Hymn 734 Ndi mkate wanu, Yesu
  • Hymn 791 Anthu opembedzawo
  • Hymn 468 Ife tikondana nanu,
  • Hymn 581 Mtiphunzitse bwinotu,
  • Hymn 375 Zipatso zakezi
  • Hymn 889 Pemphera m’mbanda kucha,
  • Hymn 1237 Ine kanthu ndilibe
  • Hymn 622 Tiyamikira ‘Tate,
  • Hymn 1149 Chete! Chete!
  • Hymn 87 IDZANI nonse ’nu
  • Hymn 404 Dzuwa la lero lonseli
  • Hymn 636 Yehova Mlungu wathu,
  • Hymn 1678 Yesu nkana saoneka, Aleluya,
  • Hymn 1427 Penyetsetsa Yesu,
  • Hymn 366 MADZULO aja kalero
  • Hymn 333 M’DZIKO lino tikhalamo
  • Hymn 257 Ndinasiya amayi,
  • Hymn 1733 Adzabwera Iyenso
  • Hymn 1607 Yesu, dzina ndi lomweli
  • Hymn 759 Ndilawako tsopanoli
  • Hymn 200 Ndi tsopano tilindira
  • Hymn 1822 Lawani chikondano chake;
  • Hymn 421 Ine ndine mlendo
  • Hymn 235 ADALITSIKA munthuyo,
  • Hymn 169 M’manda nagonamo
  • Hymn 1085 “Khala mwa Ine,” ndinu mwini mphamvu,
  • Hymn 284 Yesu Mfumu Inu
  • Hymn 748 Ndiye wa moyo wonse Mwiniyo,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version