Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 30 YEHOVA, Mbusa wangadi,

  1. Home   »  
  2. Hymn 30 YEHOVA, Mbusa wangadi,

Hymn 30 YEHOVA, Mbusa wangadi,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 30 YEHOVA, Mbusa wangadi,

 

YEHOVA, Mbusa wangadi,
Ndilibe kusoŵa;
Andigonetsa bwinoli
Mumsipu wokoma.

Ku madzi ake odikha
Anditsogolera;
Ndi moyo wanga wofoka
Aulimbikitsa.

Anditsogolera m’njira
Zakulungamazo;
Chifukwa changa ay’, koma
Cha dzina lakelo.

Ndipyola kodi chikhwaŵa
Cha mthunzi wa imfa?
Ndilibe mantha ngati ’Nu
Mundiperekeza.

Chakudya changa chabwino
Mwandikonzera pha!
Pamaso pa adaniwo
Mudyetsa mtimanga.

Mwadzoza mutu wanga ndi
Mafuta okoma;
Mwadzadza chikho changadi,
Inde, chisefuka.

Zokoma ndi zakuyanja
Zidzanditsatako;
Ndikhala m’nyumba ya Mlungu
Ku nthaŵi zonsezo.

Post navigation

Previous: Hymn 29 CHIKONDI cha
Next: Hymn 31 MULUNGU Wamkulu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 486 MPULUMUTSI Yesu,
  • Hymn 260 ODALA ndi onsewo,
  • Hymn 1154 Zakutsogolo sitidziwa ‘yi;
  • Hymn 1640 Alinkudza Ambuye Yesu
  • Hymn 1211 Mwakhulupiriradi
  • Hymn 27 “Msanga ndidzabweratu,
  • Hymn 925 Kodi umadandaula:
  • Hymn 1108 Khala chete mtima wanga,
  • Hymn 250 Lidze msanga dzuwa lanu
  • Hymn 1398 Nditama mphamvu yake
  • Hymn 463 Yesu atiuza tiwale ‘fe,
  • Hymn 126 DAVIDE kubusa kuja,
  • Hymn 1130 Mbuyanga Yesu, mundigwire dzanja
  • Hymn 1677 Zomkweza zili m’Mwamba,Aleluya
  • Hymn 504 Pakumyamika Iye
  • Hymn 138 Kumva ulikumva, ulikumva,
  • Hymn 336 Perekani mtima wanu
  • Hymn 1366 Sititha ifedi
  • Hymn 1688 Mulibe m’mandamu,
  • Hymn 261 Munafera pa mtanda
  • Hymn 1068 Ambuye, thandizenitu
  • Hymn 735 Mwa chikho chokumbutsa
  • Hymn 1543 Idzani, Mzimu Inu,
  • Hymn 81 Imva mawu akewo,
  • Hymn 668 Achisoni, obvutidwa,
  • Hymn 1522 Tikaona bvuto,
  • Hymn 899 ‘Tate wa Kumwambako,
  • Hymn 1116 Kwawo kwa Mbuyako
  • Hymn 1151 Pomulambira Yesu Mbuyanga,
  • Hymn 194 AMBUYE’naitan’ne;
  • Hymn 1500 Simbani Mbiri yomwe,
  • Hymn 1700 Ambuye Mwini moyo,
  • Hymn 19 MULUNGU akhale nawo,
  • Hymn 1030 Tioperanji ifetu?
  • Hymn 952 Ndimayenda paulendo,
  • Hymn 751 Mongatu mawu anuwo,
  • Hymn 273 Mlungu akuyang’aniredi
  • Hymn 1472 Ona! Ona! Onatu!
  • Hymn 223 ATI Yesu Mbuyeyo:
  • Hymn 586 Yesu Mfumu,
  • Hymn 254 PAMENE ndisawuka,
  • Hymn 1159 Mwalembedwa mukalata
  • Hymn 839 Adani sindiopa mukalipo;
  • Hymn 444 Mpemphe Mbuye asunge
  • Hymn 1135 Mulungu anditsogolera,
  • Hymn 1484 Idzatu, idzatu
  • Hymn 187 UFUNA kuwomboledwa kodi?
  • Hymn 1300 Poyenda m’mdima bii,
  • Hymn 55 UNAKHETSEDWA mwazi do!
  • Hymn 644 M’wasunge, m’wayendetse
  • Hymn 344 ’TATE, ’Nu.
  • Hymn 473 Mzinda woyerawo!
  • Hymn 799 Inu Mlungu kalelo
  • Hymn 1513 M’Bukuli ine ndi
  • Hymn 1333 Idzatu kwa Yesuyo,
  • Hymn 544 Zoopsya sitidziwapo
  • Hymn 1778 Angelo kwezani
  • Hymn 564 Ndi chifukwa atikonda,
  • Hymn 1743 M’kati mwa zobvuta zathu
  • Hymn 104 MUBWERE Mzimu Inu

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version