Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 266 MBUYE ndamva mwawazira

  1. Home   »  
  2. Hymn 266 MBUYE ndamva mwawazira

Hymn 266 MBUYE ndamva mwawazira

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 266 MBUYE ndamva mwawazira

 

MBUYE ndamva mwawazira
Anthu ena madalitso;
Mvula yanu yawagwera;
Mbuye, ine mudalitse.

Etu ine, etu ine,
Mbuye, ine mudalitse.

’Tate, msandipitirire,
Ndimaipa mtima ine;
Ndiyenera munditaye,
Koma mukhululukire.

Yesu, msandipitirire
Kuti ndinu ndikondane;
Ndinalira Inu Mbuye,
Msandileke poitana.

Mzimu, msandipitirire,
Mupenyetsatu akhungu
Mboniyo ya Mbuye Yesu,
Mundipatse ine mphamvu.

Ndinagona mwa zoipa,
Ndinakunyozani ine,
Dziko lino ndinakonda,
Mbuye, mukhululukire.

Ha! chikondi cha Mulungu,
Mwazi wa Mbuyathu Yesu,
Chiyanjano cha Mzimuyo
Zonse zidzalemekeza.

Post navigation

Previous: Hymn 260 ODALA ndi onsewo,
Next: Hymn 281 MBUYE, mwatiuza ’fe

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 237 SINDINANYENGEDWA konse
  • Hymn 1666 Yesu, ndinutu chitsime
  • Hymn 1251 Ndasokera m’tali ndithu
  • Hymn 78 ALINKUDZA wansoni Munthu,
  • Hymn 239 TILI ndi mtendere
  • Hymn 478 YESU atiuza tiŵale ’fe.
  • Hymn 444 Mpemphe Mbuye asunge
  • Hymn 220 Kalekale ndinathawa,
  • Hymn 1177 Ndidziwitsitsa Yesu ndi wanga,
  • Hymn 1196 E! chikondi ndithu,
  • Hymn 135 Kudziwa ukudziwa,
  • Hymn 611 Tidzakhala naye nthawi zonse ndi kuimbako,
  • Hymn 722 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 1162 Mumvetu abwenzi athu,
  • Hymn 1465 Akulu inu m’bwere nonse,
  • Hymn 1041 Zosauka unvomere,
  • Hymn 1618 Anakwera,
  • Hymn 500 >AMEN, Amen, Amen.
  • Hymn 119 Tamverani anthu inu,
  • Hymn 251 NDIFUNA Yesuyo,
  • Hymn 1626 Mbuye Yesu adzabwera,
  • Hymn 1572 Mumbveke, mbveke, mbveke,
  • Hymn 1207 Poyambapo ndakondwadi,
  • Hymn 435 ANAKWATIRA kale
  • Hello world!
  • Hymn 367 MPULUMUTSI, tikagona
  • Hymn 457 KALE m’mzinda wachifumu
  • Hymn 668 Achisoni, obvutidwa,
  • Hymn 1255 Chitha nchiani kund’yeretsa?
  • Hymn 414 Ana ake adzapuma
  • Hymn 594 Monga may’ asusuza
  • Hymn 1184 Akondwerera nthawiyi
  • Hymn 674 Anthu onse taukani,
  • Hymn 1698 Chinkana dziko lonselo
  • Hymn 206 YESU, mulikundipempha
  • Hymn 404 YANG’ANA mtanda wa Yesu,
  • Hymn 321 Ndi ponse paphiri ndi padambopo
  • Hymn 1020 Ngati umtsata Mpulumutsi wakoyo,
  • Hymn 79 Mlendo ali pakhomo,
  • Hymn 646 Mudalitse nyumba yathu;
  • Hymn 812 Ndi ena sanamvera ‘yi,
  • Hymn 1170 Pamtanda wake
  • Hymn 1691 Lero Kristu anauka, Aleluya,
  • Hymn 586 Yesu Mfumu,
  • Hymn 733 Ndimamva ludzu Yesu,
  • Hymn 1380 Tilemekezetu
  • Hymn 1007 M’mene umauka m’mawa,
  • Hymn 183 Mlemekeze, bukitsani,
  • Hymn 496 Yesu Mbuye ‘Nu wabwino,
  • Hymn 944 Tiyeni nonsenu okonda Yesuyo,
  • Hymn 998 Anatilemba Yesu tikagwire nkhondo yake,
  • Hymn 603 Mzimu wanu Wakuyera,
  • Hymn 176 AITANA, aitana dziko lonse,
  • Hymn 485 POMPANO pandikonda
  • Hymn 492 Yesu Mbuye ‘Nu wafatsa
  • Hymn 159 Kamwana Yesu ‘nabadwa,
  • Hymn 378 Ku madzi ake odikha
  • Hymn 281 MBUYE, mwatiuza ’fe
  • Hymn 271 Pomwalira Mbuyeyo
  • Hymn 1715 Kodi misozi itisowa,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version