Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 239 TILI ndi mtendere

  1. Home   »  
  2. Hymn 239 TILI ndi mtendere

Hymn 239 TILI ndi mtendere

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 239 TILI ndi mtendere

 

TILI ndi mtendere
Wopambanatu,
Monga ngati mtsinje
Mumitimamo;
Koma mtsinje uno
Umayenda phee,
Nthaŵi zonse mtima
Nutonthozabe.

Tikakhulupira
Mlungu wathuyo,
Tidzaona mwayi
Ndi mtenderewo.

Dzanja la Mulungu
Litisunga nji!
Nkhondo ya Satana
Sitiopa ’yi.
Zaphokoso zonse
Ndi zoopsyazo
Sizibvuta mtima,
Siziloŵamo.

Masauko athu
Ndi zokondwazo,
Azilola zonse
Ndi Atatewo.
Pokhulupirira
Tidzapezabe
Kuti mtima wake
Utikonda ’fe.

YESU ndiye Mbuye wanga,
Ndamva Mawu akewo
Andilandira ine,
Nandipulumutsatu.
Mwalembedwa mukalata
Mawu ake omwewo,
Kuti iwo akumvera
Akalandiridwatu.

Ndinakahala wakuipa, Ndinamkana kalelo;
Koma Yesu waiŵala
Mphulupulu zangazo.

Wapumitsa mtima wanga,
Kaamba ndaphunziratu
Mau ake olembedwa
Mukalata mwakemo.

Mumvetu abwenzi athu,
Musakanirire ’yi;
Yesu aitana inu,
Zalembedwa zomwezi.

Post navigation

Previous: Hymn 220 MULUNGU mundichitire chifundo,
Next: Hymn 241 MTENDERE uli m’mtima mwathumu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 232 Uchita kwombola,
  • Hymn 482 Ndinu wakuyera,
  • Hymn 226 BWENZI ndinamkomanayo
  • Hymn 1843 Chigwa choopsacho cha imfa ndikachilowera,
  • Hymn 1063 Pokhala mtendere mu mtimangamu,
  • Hymn 355 DZIKO lonse mlambire
  • Hymn 572 Anadza nazo mphatso zake
  • Hymn 1569 Mtima wodetsa mukonzere,
  • Hymn 262 “KHALA mwa Ine,” Yesu anatero;
  • Hymn 137 UTHENGA wa Ambuye
  • Hymn 428 Tiyandika, Mbuye,
  • Hymn 12 Kumva milandu yathu mudzabwera
  • Hymn 886 Chikondi, chimwemwe,
  • Hymn 1366 Sititha ifedi
  • Hymn 619 Tilimalima m’minda,
  • Hymn 1612 Adzadza indetu
  • Hymn 1247 A Chikondi chopambana,
  • Hymn 305 M’mwazi wake tisambamo;
  • Hymn 121 Imbira!
  • Hymn 981 Tiyeni Akristu,
  • Hymn 665 Pomangidwa anthu nayo
  • Hymn 188 MPULUMUTSI Wokondedwa,
  • Hymn 1238 M’mene ndifa inedi,
  • Hymn 653 Nditsogolere m’njirayi
  • Hymn 1631 Mudzabwera, mudzabwera;
  • Hymn 1830 Ndiye M’busa wanga
  • Hymn 228 MWAKHULUPIRIRADI
  • Hymn 1079 Khalatu woyera,
  • Hymn 792 Dzuwa la Mulungu
  • Hymn 1533 Ndipatsa inu mtimawu,
  • Hymn 1754 Ndiye akumbukira
  • Hymn 1291 Njobvuta njira ndimayendamo,
  • Hymn 1607 Yesu, dzina ndi lomweli
  • Hymn 895 Ndikabwera ndi katundu
  • Hymn 1253 Ndingopatsa Inu Mbuye
  • Hymn 1059 Kalelo m’mtima ndinakondwa,
  • Hymn 672 Mbwere Yesu Mwini moyo,
  • Hymn 309 ANA akumwamba ndife,
  • Hymn 984 Mpingo wa Mulungu
  • Hymn 211 Chakudya ichi ndi cha iwenso,
  • Hymn 19 MULUNGU akhale nawo,
  • Hymn 411 Yesu adza kukundika
  • Hymn 114 NDIPO Eliya anati kwa Elisa:
  • Hymn 450 YESU, munditsogoza
  • Hymn 303 Ona pamtanda Yesuyo
  • Hymn 54 Dalitsani mafuko onse,
  • Hymn 699 Inu wakudzatu
  • Hymn 1733 Adzabwera Iyenso
  • Hymn 1823 Opani Iye, nimuleke
  • Hymn 623 Mbuye, tikuthokozani,
  • Hymn 396 PETURO ’nafunsa Hananiya:
  • Hymn 722 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 312 NDIMAYENDA paulendo
  • Hymn 448 Yesu ndi wofatsa,
  • Hymn 662 Tisaleme pakuchita zabwinozi,
  • Hymn 1540 Pankhope pathu mthirepo
  • Hymn 94 Ndani anatiwombola?
  • Hymn 1368 Mitambo inu yakumwambako,
  • Hymn 367 Nonse okhala pansipa,
  • Hymn 565 Koma sitimpenya m’khola

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version