Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 222 NDILIKUMVA m’mtima mwanga

  1. Home   »  
  2. Hymn 222 NDILIKUMVA m’mtima mwanga

Hymn 222 NDILIKUMVA m’mtima mwanga

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 222 NDILIKUMVA m’mtima mwanga

 

NDILIKUMVA m’mtima mwanga
Mau ake a MbuyAnga,
Ati, “Ndakukonda iwe,
Kodi undikonda Ine?”

Ati; “Mwana, kumbukira
Zonse ndinakuchitira;
Ndakukonda, ndakufera,
Ndakufuna posokera.

“Ku zoipa zonse zako,
Goli la pakhosi pako,
Ndi kunthenda zosautsa
Ndine ndakupulumutsa

“Kodi mayi wobereka
Mwana wake adzamleka
Pena adzamwiŵalira,
Koma ndikukumbukira.

“Nthaŵi ilikudza yonse
Sindisinthanika konse;
Imfa sindiletsa Ine
Ndisakondekonde iwe.

“Ine ndidzakuonetsa
Zonse zakukondweretsa
Za Kumwamba zanga izo,
Mwana, sundikonda ine?”

Ambuyanga, ndalephera,
Mwachisoni ndipemphera
Mundipatse ine ndithu
Mtima wakukonda Inu.

Post navigation

Previous: Hymn 220 MULUNGU mundichitire chifundo,
Next: Hymn 241 MTENDERE uli m’mtima mwathumu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 380 Ndipyola kodi chikhwawa
  • Hymn 1058 Chimwemwe chija chamumtima
  • Hymn 640 Anakwatira kale
  • Hymn 821 Aleluya!
  • Hymn 628 E! chisomo chosaleka
  • Hymn 486 Yesu, Yesu,
  • Hymn 125 ODALA ali iwo,
  • Hymn 1584 Konda dzinalo la Yesu
  • Hymn 454 TAONANI, m’kholamo,
  • Hymn 1235 Yesu wathadi
  • Hymn 744 Kristu ndi mwini moyo wathuwu,
  • Hymn 1294 Wakuba uja nachiona,
  • Hymn 1572 Mumbveke, mbveke, mbveke,
  • Hymn 330 N’LOKOMA Dziko langa!
  • Hymn 524 Wokoma Mbuyathu
  • Hymn 1019 Tsata, tsata, nditsatadi Yesu;
  • Hymn 451 Yesu ndi Mbuyako,
  • Hymn 1260 Yesu, mulikundipempha, Munaterodi:
  • Hymn 485 Mukatiitana
  • Hymn 1676 Kondwerani dzuwa lino Aleluya,
  • Hymn 281 MBUYE, mwatiuza ’fe
  • Hymn 1123 Ndifuna Inu, Yesu,
  • Hymn 284 Yesu Mfumu Inu
  • Hymn 1230 Lichiza mzimu wophwetekwa ukakhale bata,
  • Hymn 453 A! MULUNGU
  • Hymn 80 KUDZA kwa Mbuye
  • Hymn 93 Mverani mbiri yozizwitsa
  • Hymn 498 Yesu akonda,
  • Hymn 954 Mbuye andipeza lero,
  • Hymn 235 Kumwamba ndikaimbanso
  • Hymn 1179 N’kamvera Yesu ndikakondwera,
  • Hymn 247 MULUNGU anditsogolera,
  • Hymn 407 Zochimwa sizilowako,
  • Hymn 1693 Koma masauko ake Aleluya
  • Hymn 389 Ambuye, mtidalitsetu,
  • Hymn 380 ATATE, muwapenya
  • Hymn 1211 Mwakhulupiriradi
  • Hymn 1547 Mtisangalatse m’zonse,
  • Hymn 1139 Namondwe akawombabe,
  • Hymn 733 Ndimamva ludzu Yesu,
  • Hymn 1647 Kubweza inetu, kubweza inetu,
  • Hymn 452 MLUNGU, Inutu,
  • Hymn 712 Mulungu akondadi leroli
  • Hymn 161 Tibwera ndi tianato
  • Hymn 1212 Zina ndi zinanso
  • Hymn 522 Akazi anadza
  • Hymn 442 MASIKA a m’dziko Mbuye,
  • Hymn 602 Mpulumutsi wakukoma,
  • Hymn 1578 Onsewa ‘nachimwa
  • Hymn 1525 Mbuye, mtiphunzitse
  • Hymn 1124 Ndifuna Inu, Yesu,
  • Hymn 621 Wolenga ndi Yemweyo
  • Hymn 1765 Zoonazi amithenga
  • Hymn 1415 Iye anatsika m’Mwamba,
  • Hymn 889 Pemphera m’mbanda kucha,
  • Hymn 696 Ufumu wake udalitsa
  • Hymn 1353 Ambuye Yesu, Inutu
  • Hymn 1633 Adzabwera, adzabwera;
  • Hymn 1182 Chikhulupiro chomwenso
  • Hymn 869 Anatipatsa Mawu onse olimbitsa mtima;

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version