Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 104 MUBWERE Mzimu Inu

  1. Home   »  
  2. Hymn 104 MUBWERE Mzimu Inu

Hymn 104 MUBWERE Mzimu Inu

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 104 MUBWERE Mzimu Inu

 

MUBWERE Mzimu Inu
Woyera, wakufatsa,
Muchotse mdima m’mtima mwathu
Tikapenye m’maso.

Mtisangalatse m’zonse,
Ndi wachifundo Inu,
Tiyembekeze kumapazi
A Mbuyathu Yesu.

Mtitsitsimutse ife
Kuchotsa nkhaŵa zathu,
Muyatse moto wachikondi
Mu mitima yathu.

Mtitsutse titachimwa
kutilapitsa m’mtima,
Mwonetsenso chikondi chokhululukira tchimo.

Kutiyeretsa m’mtima
Ndi ntchito yanu yokha,
Kupatsa moyo watsopano
M’mene timafoka.

Mukhale m’kati mwathu,
Mutichotsere mantha,
Tidzayamika ’Tate wathu,
Mwana wawo ndi ’Nu.

Post navigation

Previous: Hymn 100 MUBWERE Mzimu Wakuyera,
Next: Hymn 121 MULUNGU, anthu ’fe

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 674 Anthu onse taukani,
  • Hymn 183 Mlemekeze, bukitsani,
  • Hymn 356 Tinafena m’nyanjamo,
  • Hymn 1627 Adzabwera, adzabwera;
  • Hymn 33 OWONADI mtima,
  • Hymn 864 Ndi chikondi mtithandize kuigwira nkhondoyi;
  • Hymn 810 Tsopano lino kwada bii,
  • Hymn 474 Yesu ndafikatu,
  • Hymn 247 MULUNGU anditsogolera,
  • Hymn 118 PANALI munthu amene,
  • Hymn 861 Mbuye, Mpingo wanu usauka kwa kukuludi;
  • Hymn 348 CHIKHULUPIRIRO chathu
  • Hymn 80 KUDZA kwa Mbuye
  • Hymn 1612 Adzadza indetu
  • Hymn 1851 Anthu onse, anthu onse,
  • Hymn 498 AMBUYE, mtidalitsetu,
  • Hymn 1695 Pokumbukira mtandawo
  • Hymn 883 Pokupempherani
  • Hymn 971 Ndinu Mbusa wanga;
  • Hymn 1430 Ndipo pakulowa
  • Hymn 107 Panalibe mwa abale
  • Hymn 348 Aitana,
  • Hymn 427 Komwe ndi chimwemwe
  • Hymn 241 MTENDERE uli m’mtima mwathumu,
  • Hymn 1616 Anafera
  • Hymn 69 KONDWERANI dzuŵa lino,
  • Hymn 1051 Zin’sowa indedi
  • Hymn 894 Mbuye, ndinu Mfumu yanga
  • Hymn 1097 Njira yanga sindidziwa,
  • Hymn 434 CHIKONDI cha Mulunguyo,
  • Hymn 378 KWEZANI mitu yanuyo,
  • Hymn 50 Akhristu nyamulani
  • Hymn 195 YESU wondikondadi,
  • Hymn 1371 Mitengo yaitalitali ‘nu
  • Hymn 1665 Nkhope yanu ndifunitsa,
  • Hymn 1217 Chisoni chonsecho
  • Hymn 191 Sindifuna Mbuye wina,
  • Hymn 1343 M’dzina la Yesuyo
  • Hymn 1702 Pakufa ine Mbuye
  • Hymn 148 PAKUPEMPHA ife pano,
  • Hymn 1137 Masiku ena pali mdima,
  • Hymn 1411 Yesu akuitanani
  • Hymn 151 UKAPENYA kwa Yesu uliko moyoko,
  • Hymn 709 Munthu aganize
  • Hymn 1022 Mbuye, nditsate bwanjiko?
  • Hymn 1205 Ndikonda chifukwa
  • Hymn 186 Kondwani nonsenu,
  • Hymn 791 Anthu opembedzawo
  • Hymn 1258 Zonse zina sizikwana,
  • Hymn 462 Pothandiza amathu,
  • Hymn 834 Tiyamike Mlungu wotipatsa zachifundozi,
  • Hymn 493 Ndimalira kwa Inutu,
  • Hymn 103 Bwenzi lathu ndinutu,
  • Hymn 139 MLUNGU anapatsa moyo,
  • Hymn 370 KWACHA lero kwati mbee,
  • Hymn 112 Pangano lake m’mwaziwo
  • Hymn 1272 Muyambe ntchito yanuyi,
  • Hymn 1655 Mbuye Yesu,
  • Hymn 1397 Okwawa pansi inu,
  • Hymn 816 Mdima wafika,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version