Hymn 936 Ukatha moyo wanga December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 936 Ukatha moyo wanga Ukatha moyo wanga Kumwamba kundichera; Dzuwalo ndimalira Lafika lokomera. Usiku m’nali mdima, Tsopano mbanda kucha; Kudzawalitsa ndithu Ku Dziko la Mulungu.