Hymn 800 Yesu munadzukanso December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 800 Yesu munadzukanso Yesu munadzukanso M’manda lero lomwetu; Ntchito munayambayo Yakudzutsa anthu ‘fe, Kuti ndi mitimayi Tigwirebe ntchitozi.