Hymn 800 Yesu munadzukanso treasurehymns 6 months ago Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 800 Yesu munadzukanso Yesu munadzukanso M’manda lero lomwetu; Ntchito munayambayo Yakudzutsa anthu ‘fe, Kuti ndi mitimayi Tigwirebe ntchitozi.