Chichewa Believers Christian Hymns
Hymn 1187 M’mitima mwathu mwakhala mbee!
M’mitima mwathu mwakhala mbee!
Mtanda wamdima wang’ambwa ke!
Panyanjapo pagawanika.
Ndife tipita ku moyo,
Mtima wabwino ndi moyo;
Kumbanda kucha kwa moyo
Kumatiuza za dzuwalo.