Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 478 YESU atiuza tiŵale ’fe.

  1. Home   »  
  2. Hymn 478 YESU atiuza tiŵale ’fe.

Hymn 478 YESU atiuza tiŵale ’fe.

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 478 YESU atiuza tiŵale ’fe.

 

YESU atiuza tiŵale ’fe.
Monga nyali m’mdima tiunike mbee!
Pansi pali mdima ŵalanitu,
Inu m’malo mwanu ndi ine ’mu.

Yesu atiuza tiyambemo,
Ationa bwino ndi kuŵalako;
Ayang’ana pansi poŵala ’fe,
Inu m’malo mwanu ndi ine ’mu.

Yesu atiuza tiŵale pa
Anthu ali m’mdima osaukawa;
Tiŵalire onse, tonsefetu,
Inu m’malo mwanu ndi ine ’mu.

Post navigation

Previous: Hymn 477 YESU, muli pa chimpando
Next: Hymn 479 ANYAMATA inutu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 83 MBUYEYO adzabwera,
  • Hymn 1807 Chithawa m’talitali
  • Hymn 35 KODI mwaona chiyani,
  • Hymn 225 Yesu akhazika
  • Hymn 1595 Ndani mwa abale athu
  • Hymn 401 A MULUNGU,
  • Hymn 1427 Penyetsetsa Yesu,
  • Hymn 348 Aitana,
  • Hymn 812 Ndi ena sanamvera ‘yi,
  • Hymn 1640 Alinkudza Ambuye Yesu
  • Hymn 43 GETSEMANI, Getsemani,
  • Hymn 252 MTIMA wa Mbuyako,
  • Hymn 1684 Mbuye mabala anu olimba
  • Hymn 535 Mbuye timlemekeze,
  • Hymn 284 Yesu Mfumu Inu
  • Hymn 1019 Tsata, tsata, nditsatadi Yesu;
  • Hymn 196 NDI inetu sinditha’yi
  • Hymn 694 Sadalekeza kuyamika
  • Hymn 1470 Chikondi cha Mbuyathu
  • Hymn 1694 Timwimbire Mlungu wathu, Aleluya
  • Hymn 318 TINALI ambiri ife,
  • Hymn 1585 Dzina ili ndi lokoma
  • Hymn 159 YESU ndi wokonda,
  • Hymn 1170 Pamtanda wake
  • Hymn 520 Tamva tikondane naye,
  • Hymn 437 MULUNGU wa Yakobo Inu, mdyetsa anthu anu,
  • Hymn 760 Usiku uja kalelo
  • Hymn 1243 Kodi mayi wobereka
  • Hymn 478 YESU atiuza tiŵale ’fe.
  • Hymn 133 Yesu watidzera, watidzera,
  • Hymn 1574 Anthu ose ndi mitundu
  • Hymn 188 Ine ndili ndi manyazi
  • Hymn 732 1 Ndinamva njala, Yesu,
  • Hymn 1826 Amadyetsa Iye mbalame zam’mwamba,
  • Hymn 773 Mtsinje woyerawo
  • Hymn 463 Yesu atiuza tiwale ‘fe,
  • Hymn 1757 Udzadziwitsa anthu
  • Hymn 117 CHOLIMBITSA mtima ndi chonditsogolera;
  • Hymn 955 Komwe ndi chimwemwe ine
  • Hymn 334 KULI dziko labwino M’mwamba,
  • Hymn 390 A! YESU, ndapangana
  • Hymn 76 Ndipereka zanga zonse
  • Hymn 58 Titasokera tinabwerera,
  • Hymn 110 MZIMU ndi mtogoleri
  • Hymn 1594 Chikondano chakechi
  • Hymn 383 KASUPE ali wodzaza
  • Hymn 1140 Paja athira Yesutu
  • Hymn 45 IFE timakufunani
  • Hymn 120 Lekani kubvutika ndi zinthu za padziko,
  • Hymn 1388 Tiimbire Mlungu wathu
  • Hymn 1462 Dzina la Yesu ndi lokoma,
  • Hymn 1690 Titama Yesuyo,
  • Hymn 409 ANTHU akum’maŵa
  • Hymn 467 NGOLIZO zilira
  • Hymn 1628 Dziko lino linaona
  • Hymn 1477 Anena anthu onsewo,
  • Hymn 1209 Mnyamata wake ndinetu,
  • Hymn 901 Musatifikitsemo
  • Hymn 284 MAVUTO ndi ambiri,
  • Hymn 372 Potero onsewo

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version