Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 455 TIIMBE ndi kulalikira

  1. Home   »  
  2. Hymn 455 TIIMBE ndi kulalikira

Hymn 455 TIIMBE ndi kulalikira

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 455 TIIMBE ndi kulalikira

 

TIIMBE ndi kulalikira
Mthenga wa chikondicho
Anamva Mlungu m’Mwambamo
Kulira kwathu pansipa.

(Ndikhulupirira Yesu
Wobadwira m’kholamo;
Iye ndiye Mfumu yathu,
Timtame nthaŵi zonse.)

Kwa ife lero anabadwa
Mwana wa Mariyayo,
Pamsinkhu, ine mng’ono koma
Mwini dziko lonseli.

Anadza nazo mphatso zake
Anatikonzeratu; Anatitseguliradi
Pakhome pa Ufumuwo.

Ambuye takutamandani
Tsiku lakubadwali,
Mwa Inu tonse tikondwera,
Tiseke tonsefe.

A! Yesu Mbuye wakuyera,
Munagona m’kholamo;
Mudzikonzere leronso
Mogona m’mtima mwangamu.

Ulemerero m’Mwambamwamba
Ndi mtendere pansipa;
Tiimbe nafe nyimboyi,
Timyamikire Mbuyathu

(Yesu ndiye Mfumu,
Yesu ndiye Mfumu!
Ndikhulupirira Yesu wobadwira m’kholamo.)

Post navigation

Previous: Hymn 454 TAONANI, m’kholamo,
Next: Hymn 456 ANA inu, ana inu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 376 Adzadalitsa ‘fe
  • Hymn 249 Amen, Amen, Amen.
  • Hymn 248 M’MENE ine ndisauka
  • Hymn 1815 Choposa nalo thupilo,
  • Hymn 973 Tigwire nkhondo yomwe
  • Hymn 1834 Chisomo ndi zokoma zake sizileka konse;
  • Hymn 1241 Ati: Mwana, kumbukira
  • Hymn 1786 Ndikonda Mlungu pomva Mbuye wanga
  • Hymn 764 “Chikho cha mwazi wangachi
  • Hymn 834 Tiyamike Mlungu wotipatsa zachifundozi,
  • Hymn 171 M’manda munalibe
  • Hymn 164 WANENA ndi Yesu,
  • Hymn 27 LEMEKEZANI Yehova,
  • Hymn 1026 Inde nditaya chumacho,
  • Hymn 31 Tamandani mbuye,
  • Hymn 410 Ana ake angonga
  • Hymn 1080 Ambuye mundisunge
  • Hymn 219 Mtenderewo wosanyenga
  • Hymn 1528 Naye Mzimu mndiphunzitse
  • Hymn 492 Yesu Mbuye ‘Nu wafatsa
  • Hymn 1378 Tsopano linoli
  • Hymn 481 Yesu wa Kumwamba,
  • Hymn 1583 Dzina la Yesuyo
  • Hymn 546 Kulibe wokwanira ‘yi
  • Hymn 499 ‘Nafera Mbuye wanga
  • Hymn 113 KALERO anthu onse
  • Hymn 536 Ana inu, myamikeni
  • Hymn 1768 Ndiye wamphamvu zonse
  • Hymn 1763 Amithenga anaimba
  • Hymn 223 Ndafoka, ndaipa,
  • Hymn 1570 Mutidziwitse ‘Tate wathu,
  • Hymn 1850 Anthu a mitundu yonse,
  • Hymn 674 Anthu onse taukani,
  • Hymn 379 Anditsogolera m’njira
  • Hymn 1537 Mulowe m’mtima, mdzazetu
  • Hymn 1311 Pothawira pena ‘yi,
  • Hymn 1018 Yesu afuna iwe unnke kwawoko,
  • Hymn 159 Kamwana Yesu ‘nabadwa,
  • Hymn 975 Tiyeni, Akristu inu,
  • Hymn 107 MUBWERE kuno Mzimu ’Nu
  • Hymn 661 Tamva aku Makedonyako atero,
  • Hymn 727 Imfa ikandifikira,
  • Hymn 755 Pamene padzakhalapo
  • Hymn 1483 Pakupempha ife pano,
  • Hymn 276 MKRISTU, ulimbike
  • Hymn 1609 Idzani nose’nu
  • Hymn 1190 Aleluya, mlemekeze,
  • Hymn 1421 Alongo ‘nu, alongo ‘nu,
  • Hymn 290 Ndi miyendo yathu iyinso njanu,
  • Hymn 1427 Penyetsetsa Yesu,
  • Hymn 1257 Mtanda m’mtima ndiyang’na,
  • Hymn 390 Lalowa dzuwa, kwada bii!
  • Hymn 1533 Ndipatsa inu mtimawu,
  • Hymn 1792 Mulungu ndiye wachifundo,
  • Hymn 200 Ndi tsopano tilindira
  • Hymn 296 TIYENI Akhristu,
  • Hymn 667 Akutopa ndi ofoka
  • Hymn 79 PAKWITANA Mbuye wanga
  • Hymn 445 Mlewe oipawo,
  • Hymn 72 Mayi watsogola ku Ulemerero,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version