Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 406 M’MENE umauka m’maŵa,

  1. Home   »  
  2. Hymn 406 M’MENE umauka m’maŵa,

Hymn 406 M’MENE umauka m’maŵa,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 406 M’MENE umauka m’maŵa,

 

M’MENE umauka m’maŵa,
Sunagwire ntchitozo,
Sunayambe kukayenda,
Ugwadire Mlunguyo.
Pena uli kusekera,
Pena nkhaŵa m’mtimamo,
Wachimwemwe, wachisoni,
Uza Yesu zonsezo.

Wakuchezacheza naye
Ukagwira ntchitozo;
Pakukumbukira Yesu,
Nkhaŵa zidzachokanso
Ndi zapansi zikafuna
Kukudzaza m’mtimamo,
Utsogole kopemphera,
Uza Yesu zonsezo.

Ndi m’kutero udzadziŵa
Chifuniro chakecho; Iye adzakuthandiza
Uthangate enanso:
Ndi ofoka ulimbitse,
Akulapa bwezatu;
Ndi za ntchito zake izi
Uza Yesu zonsezo.

Ndipo ngati ungolema,
Ulefuka m’dzulomo,
Ndi Satana akayesa
Kukukola m’mtimamo:
Wakufoka, wakuopa,
Penyetsetsa Iyeyo;
Udzakhazikika m’mtima
Pakumuza zonsezo.

Post navigation

Previous: Hymn 405 POLENGA dzikoli
Next: Hymn 407 ADZAPAMBANA Yesu ponse

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 303 Ona pamtanda Yesuyo
  • Hymn 727 Imfa ikandifikira,
  • Hymn 109 Chiyembekezo changacho
  • Hymn 315 YENDANI munjira yake,
  • Hymn 1566 Mufike monga ngati mphepo yokokomayo,
  • Hymn 1615 Anakonda,
  • Hymn 341 PAKUPEMPHERATU
  • Hymn 1133 Ngatitu abwenzi anga
  • Hymn 388 Ambuye, Mzimu wanu
  • Hymn 178 ZAMBIRI zogona m’kholamo,
  • Hymn 429 M’DZANJA lanu Ambuye,
  • Hymn 521 Apunzitsi, ana omwe,
  • Hymn 1318 Ndibwera kwa Ambuyeyo,
  • Hymn 1377 Ndi amithenga akumwambako,
  • Hymn 927 Pakutsazikana nanu
  • Hymn 432 KRISTU ndiye Mwala wathu,
  • Hymn 1256 Chitsime ndi chokoma
  • Hymn 226 BWENZI ndinamkomanayo
  • Hymn 310 Tafika kwa inu mutiunikire,
  • Hymn 1348 Akupeza, akupeza,
  • Hymn 237 Munasiyatu
  • Hymn 1096 Tifuna Inu, Mbuye,
  • Hymn 1287 Wadza Yesu wandidzoza,
  • Hymn 393 Tilikuimba nyimbo yomweyi,
  • Hymn 288 Ndi maso athu awa nawo nganu,
  • Hymn 902 Ndikondwa kuganizabe
  • Hymn 401 A MULUNGU,
  • Hymn 482 TCHIMO musalole, musadziipitse,
  • Hymn 438 Yesu ndiye Mbusa
  • Hymn 201 NDILINKUDZA kwa Ambuye,
  • Hymn 255 KHALA chete mtima wanga
  • Hymn 203 NTHAWI yathadi bwerera mbale,
  • Hymn 583 Anabadwa,
  • Hymn 427 AULENDO amayenda
  • Hymn 598 Mlungu ali nane;
  • Hymn 915 Mumzinda wa Mulungu
  • Hymn 467 Ife ana sitiopa,
  • Hymn 1666 Yesu, ndinutu chitsime
  • Hymn 74 Ndipereka zanga zonse
  • Hymn 802 Ndife anthu aulendo,
  • Hymn 496 Yesu Mbuye ‘Nu wabwino,
  • Hymn 1398 Nditama mphamvu yake
  • Hymn 1169 Mwazi wa Yesu
  • Hymn 788 Moyo watsopano
  • Hymn 1396 Ndi maso Ambuyathu
  • Hymn 1424 Malo anachepa,
  • Hymn 871 Tiphatikane tonsefe okonda Yesu Kristu;
  • Hymn 1404 “Undipatsetu
  • Hymn 809 Madzulo aja kalelo
  • Hymn 1485 Unachimwachimwa ndithu,
  • Hymn 150 MIPINGO iyo idzatu,
  • Hymn 1677 Zomkweza zili m’Mwamba,Aleluya
  • Hymn 1215 Ndimkonde Kristuyo,
  • Hymn 1456 Pakuti anthu akumvera
  • Hymn 384 USIKU uja kalero,
  • Hymn 7 “Mbuye Woyera! E, Woyeranokha!
  • Hymn 1159 Mwalembedwa mukalata
  • Hymn 153 NDAKUMANA ndi bwenzi lokomalo,
  • Hymn 1221 Bwenzi ndinamkomanayo,
  • Hymn 1002 Haya! ‘Nzanga taonani Yoonekayo

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version