Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 390 A! YESU, ndapangana

  1. Home   »  
  2. Hymn 390 A! YESU, ndapangana

Hymn 390 A! YESU, ndapangana

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 390 A! YESU, ndapangana

 

A! YESU, ndapangana
Kutumikira ’Nu
Ndi moyo wanga wonse,
Mbuyanga ndinutu;
Mukhaletu pafupi
Masiku onsewo,
Sindidzaopa konse,
Mutsogolereko.

Ndikufuna kumva Inu,
E, Mawu anuwo,
Ndisamve za satana
Zonyenga zakezo;
Adani anga onse
Andizingiratu;
Mukhaletu pafupi,
Mundithangate ’Nu.

A! Yesu mwapangana
Ndi anthu anuwo
Adzakhala ndinu
Ku Dziko lanulo;
Inenso ndapangana
Ndisabwerere ’yi;
Mndipatse mphamvu yanu
Ambuye ndinudi.

Mundionetse, Yesu,
Mapazi anuwo,
Ndidzapondera awa
Munjira monsemo;
Ndithangateni ine
Ndisalefuke ’yi;
Mundilandire m’Mwamba
Ndikamwaliradi.

Post navigation

Previous: Hymn 389 NDIMAMVA njala, Yesu,
Next: Hymn 391 MUNDIMVERE, Mbuye wanga

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 741 Chakudya ichi chidzapita du,
  • Hymn 1487 Bvumbulutsa zonse zako
  • Hymn 1748 Ambuye tsopano lino,
  • Hymn 418 UDINDO wolalikira Uthenga,
  • Hymn 1652 Mabala ajawo
  • Hymn 21 Mbuye mtsitsimutse!
  • Hymn 340 Imvani,
  • Hymn 976 Muyendenso kunka komwe,
  • Hymn 81 Imva mawu akewo,
  • Hymn 926 Mbale wako unamkonda,
  • Hymn 1152 Pokonda Yesuyo, mtendere!
  • Hymn 1381 Ndi mitima yokondwera
  • Hymn 1765 Zoonazi amithenga
  • Hymn 743 Mudze, anthuni, talawani ‘nu
  • Hymn 1208 Kalelo! Kalelo!
  • Hymn 389 NDIMAMVA njala, Yesu,
  • Hymn 157 INU nonse ovutidwa,
  • Hymn 1470 Chikondi cha Mbuyathu
  • Hymn 401 Dzuwa la lero lonseli
  • Hymn 497 TILIKUIMBA nyimbo yomweyi,
  • Hymn 1570 Mutidziwitse ‘Tate wathu,
  • Hymn 611 Tidzakhala naye nthawi zonse ndi kuimbako,
  • Hymn 121 MULUNGU, anthu ’fe
  • Hymn 690 Mu ulemerero,
  • Hymn 719 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 1112 Masiku anga onse
  • Hymn 816 Mdima wafika,
  • Hymn 1803 Nowayo nayendamo,
  • Hymn 1670 Bwenzi ndiye wakufera,
  • Hymn 1545 Mundilimbitse m’mtima
  • Hymn 537 Aleluya! Aleluya!
  • Hymn 322 Walira Yesu m’dziko linoli,
  • Hymn 250 Lidze msanga dzuwa lanu
  • Hymn 721 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 27 LEMEKEZANI Yehova,
  • Hymn 198 CHITSIMECHO cha mwaziwo
  • Hymn 400 Dzuwa liwala, m’tulotu
  • Hymn 1742 Yesu ndinu moyo wathu,
  • Hymn 191 Sindifuna Mbuye wina,
  • Hymn 35 Zonse za m’dziko zidzatha,
  • Hymn 110 MZIMU ndi mtogoleri
  • Hymn 1304 Ndi ine sizitheka ‘yi
  • Hymn 654 Ndilimbikitse, Mbuye, nji!
  • Hymn 480 Tifunitsa Inu tere,
  • Hymn 1012 Ndi zipatsozo,
  • Hymn 1077 Khalatu woyera,
  • Hymn 322 PAKUYITANIDWA munthu pa dziko ino,
  • Hymn 268 POKHALA mtendere mu mtimangamu,
  • Hymn 331 NDILI ndi kwathu ine,
  • Hymn 403 NDIYIMBA ndi chimwemwe lero,
  • Hymn 181 Zonse ndinakonda kale
  • Hymn 1140 Paja athira Yesutu
  • Hymn 1334 Walandira inetu
  • Hymn 350 MBUYE ndayima pano,
  • Hymn 1558 Wosangalatsa, ine ndikalira
  • Hymn 191 AMBIRI tikondwera mwa Yesu,
  • Hymn 1372 Zam’madzi zonse zakuopsyazo,
  • Hymn 144 Yesu, ndipemphera
  • Hymn 399 Tchimo lathu lonse, Yesu,
  • Hymn 648 Mulungu wa Kumwamba,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version