Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 372 DZUŴA la Mulungu

  1. Home   »  
  2. Hymn 372 DZUŴA la Mulungu

Hymn 372 DZUŴA la Mulungu

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 372 DZUŴA la Mulungu

 

DZUŴA la Mulungu
Ladzatu labwino;
Ndi chimwemwe ife
Tiliona lero.
Lithaŵitsa nkhaŵa,
Lichotsanso mantha
Ndimo m’mtima mwathu
Likhalitsa bata.

Tikondwera kuti
Tipumula lero;
Tazileka ntchito
Kuti tipemphere.
Koma ntchito zathu
Za palero lino
Nzakumvera Yesu,
Kumlandira bwino.

Post navigation

Previous: Hymn 371 AMBUYE, tasonkhana
Next: Hymn 373 NYUMBA ya Mulungu, ili pano,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 261 Munafera pa mtanda
  • Hymn 117 Atate wondipatsazo,
  • Hymn 329 Yesu atonthoza mtima
  • Hymn 206 YESU, mulikundipempha
  • Hymn 231 AMBUYE, m’imfamo
  • Hymn 278 Aweruza ndi mphamvu
  • Hymn 21 Mbuye mtsitsimutse!
  • Hymn 148 PAKUPEMPHA ife pano,
  • Hymn 1061 Mundichotsere tchimo lonse
  • Hymn 603 Mzimu wanu Wakuyera,
  • Hymn 22 MU ZONSE abale yamikani,
  • Hymn 443 Tchimo musalole,
  • Hymn 173 MWAMVA Mawu a Mulungu;
  • Hymn 1104 Mndisungire mtima wanga,
  • Hymn 524 Wokoma Mbuyathu
  • Hymn 1021 Kunsi kudambo, pena m’mwamba m’phirimo,
  • Hymn 385 Tsopano, poyamba paja,
  • Hymn 491 KWA Yesu ndi kwabwinoko,
  • Hymn 1598 Mtiphunzitse, Mbuye Yesu,
  • Hymn 67 PAMENEPO pokhala madzulo,
  • Hymn 256 NGATI mtima sumakonda
  • Hymn 38 ANGELO ayimba,
  • Hymn 956 Mbuye munditsogolere,
  • Hymn 983 Nkhondo ya Satana
  • Hymn 251 Kuli chimwemwe m’dzuwalo
  • Hymn 1702 Pakufa ine Mbuye
  • Hymn 1588 Wandiwombola inetu
  • Hymn 91 NDITAME Mlungu m’mtimamo,
  • Hymn 1617 Anadzuka,
  • Hymn 73 Mu ulemerero tidzakhala m’yaya,
  • Hymn 235 ADALITSIKA munthuyo,
  • Hymn 180 Ndinachita mphulupulu,
  • Hymn 724 Ndine mlendo pansi pano,
  • Hymn 1590 Mtima ndimakondweramo,
  • Hymn 526 Mnandidzera, Ambuye,
  • Hymn 473 YESU wa Kumwamba,
  • Hymn 1779 M’dzikomo Ambuye
  • Hymn 845 Ufumu wanu, Mbuye Yesu,
  • Hymn 488 M’MANJA a Yesu wanga
  • Hymn 1423 Oipa inu nonsetu,
  • Hymn 1114 Akukumbukira
  • Hymn 18 POKHALA Inu
  • Hymn 1409 Kodi mufunatu Yesu?
  • Hymn 1355 Atate, Mwana, Mzimunso,
  • Hymn 346 Aitana,
  • Hymn 1204 Ambuyanga Yesu,
  • Hymn 1452 Inu akutopawo,
  • Hymn 1752 Napulumutsa tonse
  • Hymn 939 Ambuye andisunga
  • Hymn 1263 Mbuye, ndingogonj tere, Ndibvomerapo;
  • Hymn 969 Akathira nsembe
  • Hymn 334 Tsugulani mtima wanu
  • Hymn 51 Mbuye dalitsani Afrika,
  • Hymn 1095 Mumtima wakufatsa
  • Hymn 1508 Mundinyemere ‘ne
  • Hymn 614 Adzabwera Mbuye wathu
  • Hymn 580 Mwana wakuyera ‘Nu,
  • Hymn 225 Yesu akhazika
  • Hymn 383 KASUPE ali wodzaza
  • Hymn 1624 Koma anthu onse omwe

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version