Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 127 POLUMIDWA ndi njokazo,

  1. Home   »  
  2. Hymn 127 POLUMIDWA ndi njokazo,

Hymn 127 POLUMIDWA ndi njokazo,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 127 POLUMIDWA ndi njokazo,

 

POLUMIDWA ndi njokazo,
M’chipululumo;
Aisrayeli ‘nafa,
Ambiri.

Mwachikondi Mlungu “Tate,
Nawuza Mose:
“Yamkuwa njoka upange,
Msangatu.”

Amene akayang’ane,
Njoka pamtengo;
Ngakhaletu walumidwa,
Achira.

Satana amatiluma,
Ndi uchimowo;
Mwana Mlungu natifera,
Pamtanda.

Tiyang’ane pamtandapo,
Tipulumuke;
Adzatitenga kupita,
Kwawoko.

Post navigation

Previous: Hymn 126 DAVIDE kubusa kuja,
Next: Hymn 128 ANTHU m’maiko onse

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1588 Wandiwombola inetu
  • Hymn 1030 Tioperanji ifetu?
  • Hymn 457 Palibe mwana wakuchepa
  • Hymn 409 ANTHU akum’maŵa
  • Hymn 1810 Kalelo Mbuye Yesu
  • Hymn 1486 M’dziko lino pansi pano
  • Hymn 530 Munaneneratu mawu a moyonso
  • Hymn 1521 Poyensedwa ife
  • Hymn 180 Ndinachita mphulupulu,
  • Hymn 417 M’manja a Yesu wanga
  • Hymn 1284 Kale ndinalira Inu,
  • Hymn 886 Chikondi, chimwemwe,
  • Hymn 612 Oyamika Mlungu mbwere,
  • Hymn 241 MTENDERE uli m’mtima mwathumu,
  • Hymn 1136 Mulungu anditsogolera
  • Hymn 814 Mutichiritse ifenso
  • Hymn 1216 Ndatsatatsatabe
  • Hymn 1324 M’moyo uno kunsiku
  • Hymn 28 Mbuye ndisaukadi,
  • Hymn 165 Yendanitu m’ulemudi,
  • Hymn 1354 Mzimu Woyera, m’mtimamo
  • Hymn 1115 M’munda wa Mbuyako
  • Hymn 765 Chikondi chili m’chikhomu
  • Hymn 372 DZUŴA la Mulungu
  • Hymn 871 Tiphatikane tonsefe okonda Yesu Kristu;
  • Hymn 1379 Mulungu yemweyo
  • Hymn 1332 Imba kawiri ndi kawirinso,
  • Hymn 94 Ndani anatiwombola?
  • Hymn 372 Potero onsewo
  • Hymn 301 Mwanawankhosa
  • Hymn 1499 Simbanitu mwachete
  • Hymn 200 Ndi tsopano tilindira
  • Hymn 194 AMBUYE’naitan’ne;
  • Hymn 50 Akhristu nyamulani
  • Hymn 1380 Tilemekezetu
  • Hymn 5 ATATE wa Kumwambako,
  • Hymn 782 Aleluya, aleluya,
  • Hymn 649 Inde, tikuyamikani, Atate, leroli,
  • Hymn 278 Aweruza ndi mphamvu
  • Hymn 1820 Kwezani nane Ambuyathu,
  • Hymn 273 Mlungu akuyang’aniredi
  • Hymn 1647 Kubweza inetu, kubweza inetu,
  • Hymn 272 AMBUYE, ndifuna nditsukenitu;
  • Hymn 280 YESU, afuna iwe unke kwawoko,
  • Hymn 61 A! MUTU wakuyera,
  • Hymn 229 POYAMBAPO ndakondwadi.
  • Hymn 97 Maso ndi maso ndi Kristu,
  • Hymn 216 Ndi misozi ndi chisoni
  • Hymn 1851 Anthu onse, anthu onse,
  • Hymn 420 FESANI mbewuzo,
  • Hymn 555 Mkucha wake ndaniyo
  • Hymn 391 Mufafanize m’bukumo
  • Hymn 464 Yesu atiuza tiyambemo,
  • Hymn 1112 Masiku anga onse
  • Hymn 1713 Zochimwa zanga zonsezo
  • Hymn 744 Kristu ndi mwini moyo wathuwu,
  • Hymn 251 NDIFUNA Yesuyo,
  • Hymn 1159 Mwalembedwa mukalata
  • Hymn 392 Chimwemwe chomwe mpatseko
  • Hymn 395 AMBUYE, Mwini zonsezi,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version