Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 113 KALERO anthu onse

  1. Home   »  
  2. Hymn 113 KALERO anthu onse

Hymn 113 KALERO anthu onse

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 113 KALERO anthu onse

 

KALERO anthu onse
Nachimwa kwa Mulungu
Mulungu anawona
Nawona tchimo lawo,
Nafuna kwawononga,
Nafuna kwawononga.

Mulungu anatuma,
Natuma mvula ija,
Nadzaza dziko lonse
Anafa anthu onse,
Anafa m’mvula muja,
Anafa m’mvula muja.

Mulungu anatuma,
Natuma Nowa uja,
Wamanga chombo chake,
Ndi chachitalitali,
Nowayo nayendamo,
Nowayo nayendamo.

Nowayo anatuma,
Natuma chikwangwala,
Chatsika pansi pansi,
Chosabwerera konse,
Chithaŵa m’talitali,
Chithaŵa m’talitali.

Kutuma wabwereza,
Natuma nkhunda ija,
Yatsika pamadzipo,
Yathyolatu mayani,
Yampatsa Nowa yemwe,
Yampatsa Nowa yemwe.

Kalelo Mbuye Yesu
’Nafera anthu onse,
Ndiyeyo chombo chathu,
Tikabisala mommo
Tipulumuka mommo,
Tipulumuka mommo.

Post navigation

Previous: Hymn 100 MUBWERE Mzimu Wakuyera,
Next: Hymn 121 MULUNGU, anthu ’fe

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 996 Leka zakuipa zako,
  • Hymn 186 Kondwani nonsenu,
  • Hymn 21 Mbuye mtsitsimutse!
  • Hymn 1828 Timtamande Iye ndi moyo wathunso
  • Hymn 948 Tiimbe mokondwa, misozi iume;
  • Hymn 1184 Akondwerera nthawiyi
  • Hymn 1615 Anakonda,
  • Hymn 653 Nditsogolere m’njirayi
  • Hymn 117 CHOLIMBITSA mtima ndi chonditsogolera;
  • Hymn 1855 Yesu, msandipitirire
  • Hymn 750 Yesu Mbuyathu, Inu nomwe ‘Nu,
  • Hymn 150 MIPINGO iyo idzatu,
  • Hymn 1258 Zonse zina sizikwana,
  • Hymn 1700 Ambuye Mwini moyo,
  • Hymn 80 Utsegule mtimawo,
  • Hymn 1262 Lero mtima ungolema, Usaukadi;
  • Hymn 1628 Dziko lino linaona
  • Hymn 895 Ndikabwera ndi katundu
  • Hymn 1525 Mbuye, mtiphunzitse
  • Hymn 391 Mufafanize m’bukumo
  • Hymn 238 MULUNGU wanga,
  • Hymn 1765 Zoonazi amithenga
  • Hymn 1379 Mulungu yemweyo
  • Hymn 157 Mbuye, Mzimu Woyera
  • Hymn 222 Ndilikudzatu,
  • Hymn 294 Yesu anali khanda
  • Hymn 1301 Moyo ukatha zi,
  • Hymn 1073 Mwa ine myatse moto wanu wakuyera mbuu,
  • Hymn 363 ATATE ndiyamika,
  • Hymn 1098 M’mene mantha andigwira,
  • Hymn 1596 Anamnyoza pansi pano,
  • Hymn 657 Ambuye, ndi chikondi tho!
  • Hymn 1387 Amaweta nyama zonse,
  • Hymn 1433 Lero lino ndi labwino;
  • Hymn 1003 Kanganani nkhondo yanu
  • Hymn 1813 Pochimwa anthu onsewo
  • Hymn 99 Tsopano ndimwona Iye
  • Hymn 1254 Mukhululukire ine,
  • Hymn 319 NDIDZATANI ine,
  • Hymn 108 MBUYE wondipulumutsa,
  • Hymn 411 TAMVA mawu omwewo,
  • Hymn 852 Munkhani zako zonsetu
  • Hymn 1646 M’busa wokoma ndi Mbuyangayo,
  • Hymn 460 KULI kaphiri m’talimo
  • Hymn 914 Nlokoma Dziko langa!
  • Hymn 1791 Tiimbe nyimbo zotamanda
  • Hymn 1209 Mnyamata wake ndinetu,
  • Hymn 200 YESU mundimve, ndikuliratu,
  • Hymn 712 Mulungu akondadi leroli
  • Hymn 86 Mwandipatulira ine,
  • Hymn 143 KONZA mtima iwe mbale,
  • Hymn 1359 Ndi Aleluya imbirani
  • Hymn 136 MKAZI wa ku Samariya,
  • Hymn 402 M’mtima mwangamu mlowemo,
  • Hymn 1690 Titama Yesuyo,
  • Hymn 1460 Akuti anthu akumvera
  • Hello world!
  • Hymn 403 Dzuwa liwala, m’tulotu
  • Hymn 383 Zokoma ndi zakuyanja
  • Hymn 1616 Anafera

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version