Hymn 1081 Ndikabisala mwanu December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 1081 Ndikabisala mwanu Ndikabisala mwanu Ndilibe mantha ‘yi; Ndikasungidwa kwanu Mumtima muti phee! Ndi mphamvu yanu yokha Ndiposa ‘daniwo; Chifundo chanu Mbuye Chitchinjirize ‘ne.