Chichewa Christian Hymns
Hymn 86 IYE wokhulupilira Yesu,
IYE wokhulupilira Yesu,
Ali nawo moyo;
Wosankhidwiratu malo ake,
Kumwambako ndithu.
Ine (ndidzayamika)
Ine (ndidzayamika)
Ndidzayamikatu
Mfumu (inde),
Ine (ndidzayamika)
Ine (ndidzayamika)
Ndidzayamika kosatha.
Yesu popita ananenatu,
Tsalanitu bwino;
Ngakhale mupeze mavutowo,
Mulimbike mtima.
Yesu abweranso posachedwa,
Padziko lapansi;
Kodi mbale wanga wakonzeka,
Kumulandira ‘Ye.