Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 409 ANTHU akum’maŵa

  1. Home   »  
  2. Hymn 409 ANTHU akum’maŵa

Hymn 409 ANTHU akum’maŵa

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 409 ANTHU akum’maŵa

 

ANTHU akum’maŵa
Nanka msangako,
Nzeru ’nali nazo,
Nafatsansowo;
Nanka kuli Mwana
Anabadwayo;
Anatsogozedwa
Ndi nyenyeziyo.

Anapeza Mwana
Ali m’kholamo,
Nagwadira Iwo
Mbuye wawoyo;
Anthu onse omwe
Ali pansipa,
Azitsata Mbuye
Ndi nyenyeziyo.

Mu ulemerero,
Yesu m’Mwambamo
Muli eni ake;
Anthu onsewo
Osadziŵa konse,
Akutalinso,
Akokedwe iwo
Ndi nyenyeziyo.

Akukhala kunja,
Osokeranso,
M’ŵaŵalire Mbuye,
Asagone’wo;
Amumdima omwe,
Olemedwanso,
Mtsogoleri wawo
Ndi nyenyeziyo.

Paulendo wathu
Tili pansipa,
Muŵalire tonse
Tili m’njiramo;
Mutitsogolere
Anthu tonsefe,
Mutifitse tonse
Ndi nyenyeziyo.

Post navigation

Previous: Hymn 400 ONA Mwana wa Nkhosa,
Next: Hymn 421 ANTHU ali m’mdima akuyitanitsa,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 314 E, moto wanu woyera
  • Hymn 431 AKAPANDA kumanga,
  • Hymn 1687 Alonda onsewo
  • Hymn 213 INE ndili ndi manyazi
  • Hymn 1311 Pothawira pena ‘yi,
  • Hymn 1022 Mbuye, nditsate bwanjiko?
  • Hymn 1303 Aa! Mulungu wanga,
  • Hymn 1641 Pakufika asonkhanitsa
  • Hymn 725 Munafera ine kale
  • Hymn 1556 Mzimu Woyera, mudzetu kwa ine,
  • Hymn 464 AKAZI anadza kwa Yesu ndi anawo,
  • Hymn 358 MLUNGU ali muno,
  • Hymn 1611 Nadzuka m’mandamo
  • Hymn 59 IMVANI uthenga,
  • Hymn 211 Chakudya ichi ndi cha iwenso,
  • Hymn 774 Tibatizidweko,
  • Hymn 376 PAMTANDA Mbuye anafera,
  • Hymn 301 Mwanawankhosa
  • Hymn 869 Anatipatsa Mawu onse olimbitsa mtima;
  • Hymn 88 Ufuna kuwomboledwa kodi?
  • Hymn 91 NDITAME Mlungu m’mtimamo,
  • Hymn 1620 Aleluya,
  • Hymn 996 Leka zakuipa zako,
  • Hymn 1530 Mndilimbitse ndipirire
  • Hymn 208 CHITHA n’chiyani kund’yeretsa?
  • Hymn 238 Mbuye Yesu, lowani m’mtima,
  • Hymn 881 Tili nazo zotiyesa,
  • Hymn 1544 Wakunga mwana ine,
  • Hymn 264 KHALATU woyera, pempheratu m’tseri;
  • Hymn 1621 Yang’anani anthu onse,
  • Hymn 933 M’mene imfa yathu idza,
  • Hymn 1031 Gwira zintchito zako,
  • Hymn 991 Ndi zapansi pano
  • Hymn 1656 Inu mundibisadi
  • Hymn 219 YESU Mbuyetu, mwafera
  • Hymn 1099 Sindidziwatu zamawa,
  • Hymn 179 TUMPHATUMPHA moyo wanga,
  • Hymn 172 Imfa yalephera
  • Hymn 308 Ifetu kuchimwa, Mbuye,
  • Hymn 195 Bwinoli tipita,
  • Hymn 873 Mtidzutse, Mbuyetu,
  • Hymn 657 Ambuye, ndi chikondi tho!
  • Hymn 993 Pakumalizidwa
  • Hymn 1014 Tingolira kaya,
  • Hymn 1434 Lero lino m’bale wanga,
  • Hymn 1603 Zina za Yesu m;Mwambamo,
  • Hymn 1238 M’mene ndifa inedi,
  • Hymn 1537 Mulowe m’mtima, mdzazetu
  • Hymn 1128 Mbuyanga Yesu, mundisunge ine
  • Hymn 1196 E! chikondi ndithu,
  • Hymn 1347 Akukonda, akukonda,
  • Hymn 834 Tiyamike Mlungu wotipatsa zachifundozi,
  • Hymn 344 M’watame,
  • Hymn 443 M’MAŴA tizifesa
  • Hymn 263 AMBUYE mundisunge
  • Hymn 185 Kondwani nonsenu,
  • Hymn 416 PALIBE wina Kumwamba,
  • Hymn 291 Ndi milomo yathu iyinso njanu,
  • Hymn 1713 Zochimwa zanga zonsezo
  • Hymn 1703 Zathedwa zonsetu

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version