Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 408 ABALE nonse mulindiranji?

  1. Home   »  
  2. Hymn 408 ABALE nonse mulindiranji?

Hymn 408 ABALE nonse mulindiranji?

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 408 ABALE nonse mulindiranji?

 

ABALE nonse mulindiranji?
Bweranitu kwa Yesuyo;
Ali kuyitana inu nonse,
Ndithu bweranitu.

Mvetsa mbale moyo ukutha,
Dziko lingonkabe;
Siya zonse bweratu we,
Yesu adzakondwa.

Tiyeni tonse tilimbiketu,
Kubukitsa Uthengawo;
Womwe Ambuye anadza nawo,
Tisakhale chete.

Tiyeni tifalitse mawuwo,
Tisabise Uthengawo;
Yesu anatiferatu tonse,
Kutipulumutsa.

Post navigation

Previous: Hymn 400 ONA Mwana wa Nkhosa,
Next: Hymn 421 ANTHU ali m’mdima akuyitanitsa,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 128 ANTHU m’maiko onse
  • Hymn 1553 Mpume pa inetu, Mpweya wa Mulungu,
  • Hymn 1848 Tiyamike Mlungu wathu
  • Hymn 235 Kumwamba ndikaimbanso
  • Hymn 227 Kasupe ali wodzaza
  • Hymn 1348 Akupeza, akupeza,
  • Hymn 297 Anapita nasiya
  • Hymn 195 Bwinoli tipita,
  • Hymn 206 Uzanitu abale,
  • Hymn 540 Amithenga akumwamba
  • Hymn 1111 Pamene ndilemedwa
  • Hymn 1311 Pothawira pena ‘yi,
  • Hymn 1003 Kanganani nkhondo yanu
  • Hymn 556 Ndani pachimpandocho
  • Hymn 168 NDINGANENE malilime,
  • Hymn 87 Aleluya, mwandigula,
  • Hymn 706 Tisaiwalire ‘bale
  • Hymn 548 Kale anthu m’kholamo
  • Hymn 1682 Atha masiku aja ansoni,
  • Hymn 367 Nonse okhala pansipa,
  • Hymn 434 Zondipingitsa zonse
  • Hymn 1004 A! mizimu yakuipa
  • Hymn 1047 Ambuye, chotsani zonse zomwezo
  • Hymn 105 Tiyamike Mbuye Yesu
  • Hymn 913 Kulibe gombe, nyanja,
  • Hymn 349 Aitana,
  • Hymn 26 NDIKULEMEKEZA
  • Hymn 477 YESU, muli pa chimpando
  • Hymn 466 Yesu, muli pa chimpando
  • Hymn 1469 M’kufatsa kwake komwe
  • Hymn 1377 Ndi amithenga akumwambako,
  • Hymn 267 AMBUYE, thandizenitu
  • Hymn 993 Pakumalizidwa
  • Hymn 1641 Pakufika asonkhanitsa
  • Hymn 1545 Mundilimbitse m’mtima
  • Hymn 782 Aleluya, aleluya,
  • Hymn 129 Mudze kwa Yesu, musachedwe,
  • Hymn 1726 Linadetsedwa dzuwa bii!
  • Hymn 443 M’MAŴA tizifesa
  • Hymn 587 Mutitsuke,
  • Hymn 397 Yesu Mbusa, mutimvere,
  • Hymn 346 PEMPHERO ndiko kufuna,
  • Hymn 1760 Amithenga a Mulungu
  • Hymn 1230 Lichiza mzimu wophwetekwa ukakhale bata,
  • Hymn 123 MULI ndi ludzu, idzani
  • Hymn 1631 Mudzabwera, mudzabwera;
  • Hymn 563 Ndipo Mwana uyu Yesu
  • Hymn 352 Tiyamike Mlunguyo,
  • Hymn 260 ODALA ndi onsewo,
  • Hymn 261 Munafera pa mtanda
  • Hymn 1636 Potuluka m’manda mwawo
  • Hymn 729 Ndifuna kumva Inu,
  • Hymn 965 Mundiuze, aulendo,
  • Hymn 1429 Penyetsetsa Yesu
  • Hymn 170 YESU ponong’oneza, idzanitu;
  • Hymn 1768 Ndiye wamphamvu zonse
  • Hymn 1164 Tikakhulupira
  • Hymn 1146 Khalani duu! Pakufa mnzathuyo,
  • Hymn 237 Munasiyatu
  • Hymn 1708 Pakugomedwapo

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version