Skip to content

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 387 MUDZE, anthuni, talaŵani ’nu

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 387 MUDZE, anthuni, talaŵani ’nu

 

MUDZE, anthuni, talaŵani ’nu
Mkate ndi chikhocho cha Mbuyathu.

Khristu ndi mwini moyo wathuwu,
Pamtanda anafera ifetu.

Anatifera nsembe Iyeyo,
Ndiye Wansembe wake Iyenso.

Imfa ndi mdima zinathaŵa zii!
Ndipo chisomo chikuŵala mbuu.

Tadzanitu, okhulupiradi,
Talandirani zachinsinsizi.

Ndiye wa moyo wonse Mwiniyo,
Moyo wosatha atipatsa ’fe.

Ndiye wodyetsa anthu omwewo,
Napatsa mwazi, moyo wakewo.

Yesu Mbuyathu, Inu nomwe ’Nu,
Tsopano mkhalebe ndi ifetu.

Post navigation

Previous: Hymn 386 MONGATU mawu anuwo,
Next: Hymn 388 MOMMUNO, Mbuye tionanetu,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1666 Yesu, ndinutu chitsime
  • Hymn 219 Mtenderewo wosanyenga
  • Hymn 168 NDINGANENE malilime,
  • Hymn 1731 Ife tinachimwadi,
  • Hymn 961 Mbuye anatiitana
  • Hymn 188 MPULUMUTSI Wokondedwa,
  • Hymn 394 TATENGA mphatso zotani?
  • Hymn 1649 Kutenga inetu, kutenga inetu
  • Hymn 1835 Mtima wanga lemekeza
  • Hymn 893 Mtima wanga ndikonzera,
  • Hymn 1104 Mndisungire mtima wanga,
  • Hymn 541 Ana inu, yamikani
  • Hymn 391 MUNDIMVERE, Mbuye wanga
  • Hymn 1027 Tithawiranji ifetu?
  • Hymn 911 Mokhala mokhamokha
  • Hymn 1452 Inu akutopawo,
  • Hymn 205 Pakukwera Kumwamba
  • Hymn 72 YESU wakukoma mtima,
  • Hymn 421 Ine ndine mlendo
  • Hymn 686 Imbadi za Iyeyo,
  • Hymn 1413 Ndichitenji kukapeza
  • Hymn 191 Sindifuna Mbuye wina,
  • Hymn 1178 Mawu omwewo, nyimbo yomweyi,
  • Hymn 963 Aulendo, munka kuti
  • Hymn 499 ‘Nafera Mbuye wanga
  • Hymn 1574 Anthu ose ndi mitundu
  • Hymn 1536 Ndilira Mzimu leroli,
  • Hymn 825 Mpatse ana ‘ng’ono
  • Hymn 955 Komwe ndi chimwemwe ine
  • Hymn 829 Titamadi ‘Tate,
  • Hymn 110 MZIMU ndi mtogoleri
  • Hymn 386 MONGATU mawu anuwo,
  • Hymn 952 Ndimayenda paulendo,
  • Hymn 1193 Tsopano Mulungu
  • Hymn 485 Mukatiitana
  • Hymn 3 TIMYAMIKIRE Mlunguyo,
  • Hymn 1753 Adzatipulumutsa
  • Hymn 479 Munanena mulandira
  • Hymn 47 Anthu m’maiko onse
  • Hymn 48 IMFA ya Mwana wa Mulungu,
  • Hymn 851 E, nthawi ya mamawayi
  • Hymn 1821 Angelo amazinga nyumba
  • Hymn 97 TIYAMIKE Mlunguyo,
  • Hymn 1019 Tsata, tsata, nditsatadi Yesu;
  • Hymn 402 M’mtima mwangamu mlowemo,
  • Hymn 413 Yesu ndiye Bwenzi lathu,
  • Hymn 1567 Mubwere Mzimu Wakuyera,
  • Hymn 1490 Musachitenso nthantha ‘yi,
  • Hymn 1263 Mbuye, ndingogonj tere, Ndibvomerapo;
  • Hymn 110 Ndaima nji pa Kristuyo,
  • Hymn 1722 Ambuye tikondweratu
  • Hymn 1179 N’kamvera Yesu ndikakondwera,
  • Hymn 1417 Atate ‘nu, atate ‘nu,
  • Hymn 127 POLUMIDWA ndi njokazo,
  • Hymn 31 MULUNGU Wamkulu,
  • Hymn 206 Uzanitu abale,
  • Hymn 54 Dalitsani mafuko onse,
  • Hymn 401 A MULUNGU,
  • Hymn 1589 Ndinasokera kalelo,
  • Hymn 1409 Kodi mufunatu Yesu?

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version