Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 337 PADZIKO pano tikhalira M’moyo wosauka;

  1. Home   »  
  2. Hymn 337 PADZIKO pano tikhalira M’moyo wosauka;

Hymn 337 PADZIKO pano tikhalira M’moyo wosauka;

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 337 PADZIKO pano tikhalira M’moyo wosauka;

 

PADZIKO pano tikhalira M’moyo wosauka;
Komatu kwa Mulungu kuli
Dziko lakudala;
Mbuyathu Yesu wapitako,
Iye ’natsogola;
Tidzamtsatira ife tonse,
Tsiku lomaliza.

Tiyeni, tiyeni,
Ku dziko lakudala;
Tidzafikira m’dziko ilo
Tsiku lomaliza.

Masiku tikatsala ife
M’dziko mwathu momwe
Mulungu watipatsa ntchito,
Tikazigwiritse.
Pamene zakuipa zathu
Zisautsa ife,
Tikapemphere Mbuye wathu,
Atipulumutse.

Ulendo wathu ukadzatha
Tidzafika kwathu,
Adzatifitsa ife komwe
Yesu Mbuye wathu.
Sitidzapeza masautso
M’dziko la Mulungu,
Tidzakondwera chikondwere
Nthaŵi zathu zonse.

Post navigation

Previous: Hymn 320 NDIKONDA Mlungu pomva Mbuye wanga
Next: Hymn 341 PAKUPEMPHERATU

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1755 Choti timtumikire
  • Hymn 1540 Pankhope pathu mthirepo
  • Hymn 1776 Tiyeni timgwadire
  • Hymn 985 Zonse zapadziko
  • Hymn 335 Mtembenuke mtima wanu,
  • Hymn 151 Inde, Yesu, mulandira,
  • Hymn 764 “Chikho cha mwazi wangachi
  • Hymn 1509 Mkate wamoyowo
  • Hymn 1484 Idzatu, idzatu
  • Hymn 127 POLUMIDWA ndi njokazo,
  • Hymn 42 Masiku tikatsala ife
  • Hymn 1371 Mitengo yaitalitali ‘nu
  • Hymn 317 UKATHA moyo wanga
  • Hymn 1649 Kutenga inetu, kutenga inetu
  • Hymn 43 GETSEMANI, Getsemani,
  • Hymn 276 Dziko lonse mlambire
  • Hymn 352 NONSE okhala pansipa,
  • Hymn 391 Mufafanize m’bukumo
  • Hymn 59 Tinachoka munjira ya imfa,
  • Hymn 337 ‘Tate ‘Nu,
  • Hymn 1429 Penyetsetsa Yesu
  • Hymn 1799 Mulungu atipatsa mphamvu
  • Hymn 192 ZAKEYU mkulu wa misonkho,
  • Hymn 1751 Mbuye ngwodalitsika,
  • Hymn 46 O! ufulu tigwirizane
  • Hymn 1163 Tili ndi mtendere
  • Hymn 373 Ayamikire ‘Nu
  • Hymn 1263 Mbuye, ndingogonj tere, Ndibvomerapo;
  • Hymn 3 Ndinu wakuyera!
  • Hymn 528 Amithenga ‘naimba pamlengapo,
  • Hymn 860 Nthawi yina adzadzuka
  • Hymn 878 Zokoma inde nthawizi
  • Hymn 1389 Tithawire kwa Mulungu,
  • Hymn 120 Lekani kubvutika ndi zinthu za padziko,
  • Hymn 441 MBUYE, tikuthokozani,
  • Hymn 1424 Malo anachepa,
  • Hymn 15 Mbuye, chifundo chanu chitigwere
  • Hymn 344 M’watame,
  • Hymn 1114 Akukumbukira
  • Hymn 250 Lidze msanga dzuwa lanu
  • Hymn 102 Mzimu ndi mtsogoleri
  • Hymn 1301 Moyo ukatha zi,
  • Hymn 571 Kwa ife lero anabadwa
  • Hymn 447 Usachimwe konse,
  • Hymn 312 NDIMAYENDA paulendo
  • Hymn 1060 Mubwere, Mzimu wa mpumulo
  • Hymn 205 KWA Inu Yesu ndilira,
  • Hymn 753 Getsemane ndionako
  • Hymn 1287 Wadza Yesu wandidzoza,
  • Hymn 45 IFE timakufunani
  • Hymn 489 Yesu, ndikabwera,
  • Hymn 378 Ku madzi ake odikha
  • Hymn 385 Tsopano, poyamba paja,
  • Hymn 561 Uyu ‘natsikira kuno,
  • Hymn 1699 A! Mutu wakuyera,
  • Hymn 267 Usekere moyo wanga,
  • Hymn 48 Ngakhale alemera
  • Hymn 1091 Mulamulire mtima, Yesu,
  • Hymn 1415 Iye anatsika m’Mwamba,
  • Hymn 1600 E! dzina la Yesu,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version