Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 30 YEHOVA, Mbusa wangadi,

  1. Home   »  
  2. Hymn 30 YEHOVA, Mbusa wangadi,

Hymn 30 YEHOVA, Mbusa wangadi,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 30 YEHOVA, Mbusa wangadi,

 

YEHOVA, Mbusa wangadi,
Ndilibe kusoŵa;
Andigonetsa bwinoli
Mumsipu wokoma.

Ku madzi ake odikha
Anditsogolera;
Ndi moyo wanga wofoka
Aulimbikitsa.

Anditsogolera m’njira
Zakulungamazo;
Chifukwa changa ay’, koma
Cha dzina lakelo.

Ndipyola kodi chikhwaŵa
Cha mthunzi wa imfa?
Ndilibe mantha ngati ’Nu
Mundiperekeza.

Chakudya changa chabwino
Mwandikonzera pha!
Pamaso pa adaniwo
Mudyetsa mtimanga.

Mwadzoza mutu wanga ndi
Mafuta okoma;
Mwadzadza chikho changadi,
Inde, chisefuka.

Zokoma ndi zakuyanja
Zidzanditsatako;
Ndikhala m’nyumba ya Mlungu
Ku nthaŵi zonsezo.

Post navigation

Previous: Hymn 20 CHIKONDI cha Mulungu wathu,
Next: Hymn 41 MKATI mwa zovuta zathu

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 635 Tipempha madalitso ano mpatse ife tonse;
  • Hymn 1434 Lero lino m’bale wanga,
  • Hymn 81 MBUYE Yesu adzabwera,
  • Hymn 12 Kumva milandu yathu mudzabwera
  • Hymn 162 Angelo anu asunga
  • Hymn 1724 Ambuye mthandize inetu
  • Hymn 1825 Zobvuta zoopsa ndi zosaukazi
  • Hymn 976 Muyendenso kunka komwe,
  • Hymn 515 Kuphiri la ‘Zitona,
  • Hymn 457 KALE m’mzinda wachifumu
  • Hymn 354 Tinafunafunatu,
  • Hymn 410 Ana ake angonga
  • Hymn 347 YESU, ndipemphera
  • Hymn 529 Zili nazotu nkhwimba zirombozo,
  • Hymn 127 Mwazi wake ndi chitsime changa,
  • Hymn 627 Mlungu wathu mwatifitsa
  • Hymn 803 Mulungu wanga, Dzuwatu
  • Hymn 493 Ndimalira kwa Inutu,
  • Hymn 1568 Kudzoza kwanu kutipatsa
  • Hymn 1246 Ambuyanga, ndalephera,
  • Hymn 293 Tidziperekadi konse kwa Inu
  • Hymn 123 Koma mudzisungire chuma cha Kumwamba
  • Hymn 521 Apunzitsi, ana omwe,
  • Hymn 219 Mtenderewo wosanyenga
  • Hymn 1257 Mtanda m’mtima ndiyang’na,
  • Hymn 537 Aleluya! Aleluya!
  • Hymn 1581 Ndi nyimbo yabwino
  • Hymn 1144 Khalani duu! Ambuye adzatu;
  • Hymn 1634 Pakwitana Mbuye wanga
  • Hymn 1349 Salephera, salephera,
  • Hymn 421 ANTHU ali m’mdima akuyitanitsa,
  • Hymn 517 “Osana m’Mwambamwamba!”
  • Hymn 74 Ndipereka zanga zonse
  • Hymn 84 LIDZE msanga dzuŵa lanu
  • Hymn 1372 Zam’madzi zonse zakuopsyazo,
  • Hymn 1584 Konda dzinalo la Yesu
  • Hymn 466 OSANATU, osana,
  • Hymn 1653 Mulungu ali wokhulula mtimatu,
  • Hymn 928 Usalire; Mpulumutsi
  • Hymn 1463 Zoipa zakhululukidwa,
  • Hymn 1207 Poyambapo ndakondwadi,
  • Hymn 1608 Yesu, dzina lakukonda
  • Hymn 479 ANYAMATA inutu,
  • Hymn 1554 Mpume pa inetu, Mpweya wa Mulungu,
  • Hymn 710 Nthano ya Hananiyayo
  • Hymn 1326 A! Mbusa wathu amvatu
  • Hymn 153 NDAKUMANA ndi bwenzi lokomalo,
  • Hymn 554 Iye ndani pamtanda
  • Hymn 250 Lidze msanga dzuwa lanu
  • Hymn 429 M’DZANJA lanu Ambuye,
  • Hymn 361 AMBUYE munapatsa tsiku
  • Hymn 580 Mwana wakuyera ‘Nu,
  • Hymn 1731 Ife tinachimwadi,
  • Hymn 553 M’munda muja ndaniyo
  • Hymn 1613 A Mulungu
  • Hymn 373 NYUMBA ya Mulungu, ili pano,
  • Hymn 1182 Chikhulupiro chomwenso
  • Hymn 997 Mawu ake atipatsa
  • Hymn 1491 Zokandweretsa m’dzikomu
  • Hymn 1598 Mtiphunzitse, Mbuye Yesu,

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version