Skip to content

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 160 MADALITSO ngati mvumbi,

  1. Home   »  
  2. Hymn 160 MADALITSO ngati mvumbi,

Hymn 160 MADALITSO ngati mvumbi,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 160 MADALITSO ngati mvumbi,

 

MADALITSO ngati mvumbi,
Pangano la chikondi;
Nyengo yakupatsa mphamvu,
Yochokera Kumwamba.

Tipempha Inu,
Mvula ya madalitso;
Nsinsi zitigwere ife,
Tipempha madalitso.

Madalitso ngati mvumbi,
Mvumbiwo ugwe lero;
M’mapiri ndi m’madambonso,
Wochokera Kumwamba.

Post navigation

Previous: Hymn 159 YESU ndi wokonda,
Next: Hymn 161 LERO lino mbale wanga,

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 565 Koma sitimpenya m’khola
  • Hymn 1111 Pamene ndilemedwa
  • Hymn 1470 Chikondi cha Mbuyathu
  • Hymn 205 Pakukwera Kumwamba
  • Hymn 811 Wopulumutsa mudzetu;
  • Hymn 234 IMFA ndi mfumu ya mdimawo,
  • Hymn 246 NAMONDWE akawombabe,
  • Hymn 1028 Yendani bwino m’njiramo
  • Hymn 913 Kulibe gombe, nyanja,
  • Hymn 501 Yesu andikonda ine;
  • Hymn 1835 Mtima wanga lemekeza
  • Hymn 611 Tidzakhala naye nthawi zonse ndi kuimbako,
  • Hymn 116 MBUYE, Mawu anu
  • Hymn 634 Mtifungatire ndi mapiko paulendo pathu,
  • Hymn 267 Usekere moyo wanga,
  • Hymn 92 KONDA dzinalo la Yesu,
  • Hymn 553 M’munda muja ndaniyo
  • Hymn 1395 Mulungu ali nane!
  • Hymn 402 BWERANITU, bweranitu,
  • Hymn 1144 Khalani duu! Ambuye adzatu;
  • Hymn 1609 Idzani nose’nu
  • Hymn 387 MUDZE, anthuni, talaŵani ’nu
  • Hymn 941 Ndi Mbuyeyo tikhalamo,
  • Hymn 665 Pomangidwa anthu nayo
  • Hymn 1378 Tsopano linoli
  • Hymn 910 Nlokoma Dziko langa!
  • Hymn 1505 Ndikampeza, ndikamtsata
  • Hymn 100 M’mene masautso onse,
  • Hymn 303 Ona pamtanda Yesuyo
  • Hymn 325 Walira Yesu wolimbitsayo,
  • Hymn 1106 Mlungu ndi wachikhalire.
  • Hymn 1418 Khulupirani kuti mukalowe m’Mwambamo,
  • Hymn 702 Mbuye wathu mutipatsa
  • Hymn 1472 Ona! Ona! Onatu!
  • Hymn 1361 Ndi Aleluya imbirani
  • Hymn 1457 Ndidziwa kuti Yesu
  • Hymn 721 Anu Mbuye ndifetu!
  • Hymn 693 Adzapambana Yesu ponse
  • Hymn 393 ZOPEREKA tiperekazi,
  • Hymn 1201 Kumwamba kwanuko
  • Hymn 38 ANGELO ayimba,
  • Hymn 1477 Anena anthu onsewo,
  • Hymn 252 M’dziko lino chimwemwecho
  • Hymn 1674 Lambira Yesuyo,
  • Hymn 1272 Muyambe ntchito yanuyi,
  • Hymn 377 Yehova, Mbusa wangadi,
  • Hymn 814 Mutichiritse ifenso
  • Hymn 773 Mtsinje woyerawo
  • Hymn 1156 Imfa ndi manda sitiopa ‘yi,
  • Hymn 988 Ndikhumba Mzimu wanu
  • Hymn 1642 M’khola mwa ng’ombe ku Betelehemu
  • Hymn 1627 Adzabwera, adzabwera;
  • Hymn 1436 Inde, lero lino Yesu
  • Hymn 443 Tchimo musalole,
  • Hymn 863 A! maliro m’Mpingo mwanu kulirira ‘balewo
  • Hymn 465 Yesu atiuza tiwale pa
  • Hymn 1682 Atha masiku aja ansoni,
  • Hymn 1744 Kale ophunzira ake
  • Hymn 525 Afike masiku
  • Hymn 826 Mutonthoze mtima

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version