Skip to content

Mon - Sat: 8.00 - 18.00

04463235323

info@example.com

Treasure Hymns – Chichewa

  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service
  • About
  • Chichewa Believers Christian Hymns List
  • Chichewa Christian Hymns List
  • Contact
  • Home
  • Privacy Policy
  • Sample Page
  • Terms and Conditions
  • Terms of Service

Hymn 119 M’BUKU la moyotu Mbuye,

  1. Home   »  
  2. Hymn 119 M’BUKU la moyotu Mbuye,

Hymn 119 M’BUKU la moyotu Mbuye,

December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Christian Hymns

Chichewa Christian Hymns

Hymn 119 M’BUKU la moyotu Mbuye,

 

M’BUKU la moyotu Mbuye,
Momwe muli, kulemba;
Tandiuzanitu Mbuye,
Ngati dzina lilimo.

Lilimo dzinali,
M’Buku lanu la moyo;
Tandiuzanitu Mbuye,
Ngati linalembedwa.

Pamene ndidza kwa Inu,
Kulapa machimowo;
M’dzandikhululukiradi,
Ndikundiyeretsanso.

Ambuye mundithandize,
Paulendo wangawu;
Pakufika kuli Inu,
Mundigwire dzanjalo.

Post navigation

Previous: Hymn 100 MUBWERE Mzimu Wakuyera,
Next: Hymn 121 MULUNGU, anthu ’fe

Leave a Reply Cancel reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Hymns You May Like

  • Hymn 1175 Sindinanyengedwa konse,
  • Hymn 1357 Mlemekeze, anakonda
  • Hymn 916 Akondwerera anthu
  • Hymn 145 Kale ndinafuna
  • Hymn 1048 Kumwamba ndiona Ambuyangayo,
  • Hymn 581 Mtiphunzitse bwinotu,
  • Hymn 467 Ife ana sitiopa,
  • Hymn 620 Mphatso zonse zathu
  • Hymn 474 MPULUMUTSI, Mbusa wathu,
  • Hymn 1232 Ambuye ndinu Mbusa, Bwenzi, ndi Wansembe wanga,
  • Hymn 821 Aleluya!
  • Hymn 390 A! YESU, ndapangana
  • Hymn 529 Zili nazotu nkhwimba zirombozo,
  • Hymn 1392 Mlungu kuona athiratu
  • Hymn 1524 Ndiwo alimbitsa
  • Hymn 1746 Mwachimwemwe, mwachisoni,
  • Hymn 1717 Mtima wangawe, uyenera
  • Hymn 106 MZIMU Woyera, mudzetu,
  • Hymn 235 ADALITSIKA munthuyo,
  • Hymn 1072 Mudzaze Yesu mtima wanga ndi chikondicho,
  • Hymn 806 Kapena wina leroli
  • Hymn 524 Wokoma Mbuyathu
  • Hymn 243 KONDWANI nonsenu,
  • Hymn 384 Mulungu akhale nawo
  • Hymn 900 Mutipatse leroli
  • Hymn 495 Wonga Inu ndikhaledi,
  • Hymn 1635 Pakwitana Mbuye wanga,
  • Hymn 60 ZATHEDWA zonsetu
  • Hymn 348 Aitana,
  • Hymn 148 PAKUPEMPHA ife pano,
  • Hymn 128 Yesu Mfumu, ine ndingadzafe
  • Hymn 417 M’manja a Yesu wanga
  • Hymn 1347 Akukonda, akukonda,
  • Hymn 973 Tigwire nkhondo yomwe
  • Hymn 650 Tikondwa tonse ndi kukuthokazani Nu
  • Hymn 1743 M’kati mwa zobvuta zathu
  • Hymn 1594 Chikondano chakechi
  • Hymn 1706 Pamutu minga kwe!
  • Hymn 1080 Ambuye mundisunge
  • Hymn 280 Tisonkhane tonsefe,
  • Hymn 1754 Ndiye akumbukira
  • Hymn 1336 Mwamva mawu a Mulungu;
  • Hymn 1821 Angelo amazinga nyumba
  • Hymn 1124 Ndifuna Inu, Yesu,
  • Hymn 178 ZAMBIRI zogona m’kholamo,
  • Hymn 359 TADZUKA mzimu wanga ‘we,
  • Hymn 228 Ataya zoipa,
  • Hymn 519 Mverani, aimba anawo,
  • Hymn 1435 Ndiwe mlendo lero lino,
  • Hymn 549 Ndiye Mbuye, Mfumu yanga,
  • Hymn 1208 Kalelo! Kalelo!
  • Hymn 621 Wolenga ndi Yemweyo
  • Hymn 1755 Choti timtumikire
  • Hymn 1204 Ambuyanga Yesu,
  • Hymn 389 NDIMAMVA njala, Yesu,
  • Hymn 642 Mulunzanitse awa,
  • Hymn 1150 Pamtanda Mbuyanga ‘nafera,
  • Hymn 1658 Idza wolema,
  • Hymn 872 Mtidzutse, Mbuyetu,
  • Hymn 793 Tikondwera kuti

Archives

  • December 2025

Categories

  • Chichewa Believers Christian Hymns
  • Chichewa Christian Hymns
  • Uncategorized
Proudly powered by WordPress | Theme: goldy-mex by inverstheme.
Go to mobile version