Hymn 730 A! Yesu mwapangana December 14, 2025 treasurehymnsChichewa Believers Christian Hymns Chichewa Believers Christian Hymns Hymn 730 A! Yesu mwapangana A! Yesu mwapangana Ndi anthu anuwo Adzakhala ndinu Ku Dziko lanulo; Inenso ndapangana Ndisabwerere ‘yi; Mndipatse mphamvu yanu Ambuye ndinudi.